Ndi Angati? by Crispy Malawi
Ndi Angati? by Crispy Malawi

Ndi Angati?

Crispy Malawi * Track #22 On MLW Tape II

The music player is only available for users with at least 1,000 points.

Ndi Angati? Lyrics

[Intro]
Ndi angati omwe amafila akamvera nyimbo za Spe? (Ndi angati?)
(Horus on the beat)
Ndi angati omwe amati akamvera ndikupanga relate? (Ndi angati?)
Ndi angati amatikonda? Ndi angati akupanga hate? (Ndi angati?)
Ndi angati angabwere ku show ya Spe ndikupayer pa gate? (Ndi angati?)

[Chorus]
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)

[Verse]
Mhu (Yeah)
Ndikudziwa mulipo ambiri koma ndungofuna figure
Ku checker numbers pa net eh! Ndikumabalalika
Ma guy kujowela wave ya audiomack ine ndikugunda mita (Mita)
Ma zaza Ndi juice mu cup eya sindikusipper liquor
Ndine street nigga ndikangotsika pa stage ukandipeza ku market
Ma plug nde ali paliponse uzingosankha ma socket
Mfana siweso ka coolest, eya usamayaluke
You just ka little kid, Spe ndi CEO link ndibwana wako ntayatsa dubi
Kodi ndili Ndi ma ex angati? Mutu mwangamu muli ma hater angati?
Ma friends angati? Satana akufuna ine nditafa
Ndi angati anakuwuza Spe akupenga?
Ukawawuze akulenga, yeah we back in business chilichonse tikutenga
Flow ya sick beat kuyipatsa matenda

[Pre-Chorus]
Ndi angati omwe amafila akamvera nyimbo za Spe? (Ndi angati?)
Ndi angati omwe akati akamvera ndikupanga relate? (Ndi angati?)
Ndi angati amatikonda? Ndi angati akupanga hate? (Ndi angati?)
Ndi angati angabwere ku show ya Spe ndikupayer pa gate? (Ndi angati?)

[Chorus]
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)
Ndi angati? (Ndi angati?)

[Outro]
Ndi angati? Tawerenganani kumeneko
Mulipo angati
Eh angati?
Angati?
Tungofuna kudziwa man tikayamba zimavuto kusiya man
Spe Ndi dealer man mukamabwera mumafunika ku dhila man

Ndi Angati? Q&A

Who wrote Ndi Angati?'s ?

Ndi Angati? was written by Crispy Malawi & Ayo Landie & Horus Dem Bad.

Who produced Ndi Angati?'s ?

Ndi Angati? was produced by Ayo Landie & Horus Dem Bad.

When did Crispy Malawi release Ndi Angati??

Crispy Malawi released Ndi Angati? on Sun Oct 08 2023.

Your Gateway to High-Quality MP3, FLAC and Lyrics
DownloadMP3FLAC.com