Album OTW by Crispy Malawi
Album OTW by Crispy Malawi

Album OTW

Crispy Malawi * Track #23 On MLW Tape II

The music player is only available for users with at least 1,000 points.

Album OTW Lyrics

[Intro]
Ndisanene fuck buddy
Company sindingapange
Ndisanene fuck buddy
Company sindingapange

[Chorus]
Wandiuza wandisowa ndati ineso
Koma ndi ineso sitingabweleranso
Anzako Umawauza Umkandikonda ineso
Koma ndi iweso Sindingayambileso
Koma Ndisaname
Mwina Titha kungokhala ma Fuck Buddies
Utha Kumandikhola Ukafuna Company
Koma Zobwelerana Nde singapange

[Verse 1]
Ndiku Dropa Tape 2 koma Album ili on The way
Ndungofuna Ndingolowa chaku Nkhatabay or Capemaclear and put my Phone away
I don’t know How, Buh i know i will find a way
Nde tandipase plan Kuti ti linky
Or ndingovunga location kuti ufike
Ndukuvaisa ku Kitchen Kuti Uphike
Kenako ukuziwa kale kuti ufile
Kuvayisa pa bar kut u sippy
Kuikora nyimbo kuti uvine
Fe fr fr fr kuti ununkhile
Zaza wezi Brain izungulire
Kwinako ukuziwa kale zoti uchite
Nde tasekeleratu usandilusire
Wabwera utatchena koma tandivulire
Another Round ima kaye ndikusutire

Album OTW Q&A

Who produced Album OTW's ?

Album OTW was produced by Ayo Landie & Mentice (MWI).

When did Crispy Malawi release Album OTW?

Crispy Malawi released Album OTW on Sun Oct 08 2023.

Your Gateway to High-Quality MP3, FLAC and Lyrics
DownloadMP3FLAC.com