Crispy Malawi
Crispy Malawi & Krazie G & Ace Dirty
Crispy Malawi
Crispy Malawi
Crispy Malawi & Virus Infectious
Crispy Malawi
Crispy Malawi & Jeff Nyimbo
Crispy Malawi & Krazie G & Ace Dirty
Crispy Malawi & Brainlock Fam
Crispy Malawi & K1-$mollet
Crispy Malawi
Crispy Malawi
Crispy Malawi & Ace Dirty & 60 Grams
Crispy Malawi
[intro:]
Ayo landie
69 grams, 60 grams
Mario brrrrr
Ace dirty
Mario brrrr (ayyyyy)
Achina Spee
Achina Spee
[Chorus]
Ndufuna cake ndi cream
Kuphaka life ndichi team
Ndili ndi ace ndi Phin
Sungatisinthe momwe tililimu
Ndufuna cash aseee, ukuti chani
It's for the gang, rest in peace to Vatycan
Ukuti bwanji ase ndili ndima guyz
Kafusefuse ma fans kuti amafeela ndani
[Verse 1: Spe, Ace]
Ndafaka flag ku ghetto, ma kicks ngati Chiukepo
Nkavala shop ndi MLW drip fukwa deal ndi bhello
Kuphusha dancehall pa easy siza pressure
If numbers don't lie sizofunika ku Qwesha
Kuyima pa stage promoter kuti payer
Iwe ukayima pa stage ndekuti uli pa Kameza
Ndizolembalemba ngati ma tatoo angawa
Amazembazemba anayamba kuthawa
Ndinene bwanji kuti ifeyo tinapitilira
Ndikhale bwanji koma akuti tuwayimilira
I can do this with my eyes closed kuyisinzinila
Ndili pa top, high spliff ndachita kuyithimisila
[Chorus:]
Ndufuna cake ndi cream
Kuphaka life ndichi team
Ndili ndi ace ndi Phin
Sungatisinthe momwe tililimu
Ndufuna cash aseee, ukuti chani
It's for the gang, rest in peace to Vatycan
Ukuti bwanji ase ndili ndima guyz
Kafusefuse ma fans kuti amafeela ndani
[Verse 2: 60 Grams]
Ndikufuna cash aseh, nigga want some bandz
A solo blunt is self care, uzi.... ndima grams
Ndangovalaso Vans ndukatrappa contraband
Ndingozidyesa ma swaz ukuziwakale plan
[Chorus:]
Ndufuna cake ndi cream
Kuphaka life ndichi team
Ndili ndi ace ndi Phin
Sungatisinthe momwe tililimu
Ndufuna cash aseee, ukuti chani
It's for the gang, rest in peace to Vatycan
Ukuti bwanji ase ndili ndima guyz
Kafusefuse ma fans kuti amafeela ndani
[Outro:]
Ayo landie!
69 grams!, 60 grams!
Mario brrrrr!
Ace dirty!
Mario brrrr! (ayyyyy)
Achina Spee!
Achina Spee!
Ace ndi Phin was written by Crispy Malawi & Ace Dirty & 60 Grams & Ayo Landie & Young Blvke.
Ace ndi Phin was produced by Ayo Landie & Young Blvke.
Crispy Malawi released Ace ndi Phin on Sun Oct 08 2023.