Witchu by Brainlock Kushizzo
Witchu by Brainlock Kushizzo

Witchu

Kushizzo * Track #15 On Shizzo From The Dizzo

The music player is only available for users with at least 1,000 points.

Witchu Lyrics

It's you that Mega

[Chorus]
I just wanna be witchu
Usandiyikiletu panja
Tizipanga zathu
Imma call you ndikasanja
I just wanna be witchu
Usandiyikiletu panja
Tizipanga zathu
Imma call you ndikasanja

[Verse 1]
Uwu Ulendo wautali uwu tandigwire mkono
Sindimvetsa from the Dizzo eya ndaona zikhomo
Maso anga patsogolo eya mbuyo sunduyan'ganako
Osalora anzakowo akulande hustle yako
Say lose ilipo [?] Mutu umagwira
Nthawi ikubwera sinzatopa kudikira
Plan yanzeru ndili nayo osandikayira
Once I get the door naweso nzakupakulira
Ndingofuna kukhale nawe
Osalora munthu wachitatu asokoneze ngini yathu ndi anthu two
Osamawamvera ndi ma hater akathoka
Angolongolora ngati mpututhu

[Chorus]
I just wanna be witchu
Usandiyikiletu panja
Tizipanga zathu
Imma call you ndikasanja
I just wanna be witchu
Usandiyikiletu panja
Tizipanga zathu
Imma call you ndikasanja

[Verse 2]
Sindimakuyiwala ndikasanja
Nanga dollar ya show iyi ndizidya ndi ndani?
Ndimakuyimbira ukaflasher
Tilipa awiri ukundivula Shati
Tiye Ku trap ukayiziwe gang
Umakhala mumtima mwanga osapayer rent
Ukhale mbali yanga usaswitche ngati kasefi
Kusiyana ndi Shizzo uzapanga nazi regret
Sindingalore uzivutika ndili bho
Imma spend my monеy witchu mthumba mukakhala bho
Ukakhala wandisowa uzingo ndimenyera call
Ndimakhala busy kuyimba nyimbo mu studio

[Chorus]
I just wanna be witchu
Usandiyikilеtu panja (Panja)
Tizipanga zathu (Zathu Zathu)
Imma call you ndikasanja (Racks)
I just wanna be witchu (Witchu Witchu)
Usandiyikiletu panja (panja)
Tizipanga zathu (Zathu Zathu)
Imma call you ndikasanja (Sanja)

[Outro]
I just wanna be witchu
Usandiyikiletu panja (Panja)
Tizipanga zathu (Zathu Zathu)
Ama call you ndikasanja (Racks)
I just wanna be witchu (Witchu Witchu)
Usandiyikiletu panja (panja)
Tizipanga zathu (Zathu Zathu)
Ama call you ndikasanja (Sanja)

Witchu Q&A

Who wrote Witchu's ?

Witchu was written by Kushizzo & Nkhiwa.

Who produced Witchu's ?

Witchu was produced by Nkhiwa.

When did Kushizzo release Witchu?

Kushizzo released Witchu on Fri Feb 16 2024.

Your Gateway to High-Quality MP3, FLAC and Lyrics
DownloadMP3FLAC.com