Kushizzo
Kushizzo
Kushizzo & Mario Bro’s (MWI) & De Zenzo
Kushizzo
Kushizzo & Nkhiwa
Kushizzo
Kushizzo & Brainlock T-Kas & Ja$per (MWI)
Kushizzo
Kushizzo
Kushizzo
Kushizzo
Kushizzo
Kushizzo & Brainlock Kizmet & Boi Sticx
Kushizzo
Kushizzo
Kushizzo & Jeff Nyimbo &
Kushizzo & Ja$per (MWI)
Kushizzo & Dirty Flo & Don.Swanky MIB
Kushizzo
Kushizzo & Nkhiwa
Kushizzo & De Zenzo
Kushizzo
[Intro]
It's Prodogy
[Chorus: Kushizzo & Nkhiwa]
Pepani nakusiyani mukudikira
Koma tape ina nditulutsa mu July
Ndili mu stu nyimbo ndikujudula
Kudya ma beat ngati ndikufutula (futula aah)
Kufuna ndizingokuona ukumwetulira (lira aah)
Uzindiwuza ndizipanga mene ukufunira (ukufunira aah)
Osandinyoza lero moyo ndiwozungulira (ndiwozungulira aah)
Uzandipeza pompa ukazungulira (ukazungulira)
[Verse 1: Nkhiwa]
Kodi mumva round (ooo oo) m'mamva ngati andigwira
Pano full sight ndikumaona njira (ooo oo)
Ukhale ndi good vibes ukandiyandikira (aah ah)
Shawty not my koma akumandipatsira (ooo oo)
Titulutsa nyimbo zina chamu July
Nkhiwa ndi Kushizzo ndima trap or die
Kuodetsa chi two litre kungonyombeka
(ooo oo) Khalifa alikutiko? Sakuwoneka
This music for my fan (ooo oo), I'm on Zero
She a rich bitch she dance ,samatha kugwira nthiko (ooo oo)
Nyimbozo in my plan , tikugwira ntchito (ooo oo)
Koma osadanda fam mumvera zi nyimbo
[Chorus: Kushizzo & Nkhiwa]
Pepani nakusiyani mukudikira
Koma tape yina nditulutsa mu July
Ndili mu stu nyimbo ndikujudula
Kudya ma beat ngati ndikufutula (futula aah)
Kufuna ndizikuona ukumwetulira (mwetulira aah)
Uzindiwuza ndizipanga Mene ukufunira (ukufunira aah)
Osandinyoza lero moyo ndiwozungulira (ndiwozungulira aah)
Uzandipeza pompa ukazungulira (ukazungulira)
[Verse 2: Kushizzo & Nkhiwa]
Sukufulumira ngati ukusochera (ukusochera)
Njira nzosiyana komwe tikulowera (tikulowera)
Ndinali pansi koma pano ndazitolera (ndazitolera)
Ndimangopanga utsi Pano nde ndakolera (ndakolera)
Ndatenga malo ndatenga bics
Ndinapanga strategize ona blueprint (Blueprint)
Akudabwa ma ghost kupanga achieve
Sinanga ankaphweketsa and we still had to believe
See me pull on a whip (Whip), Ndikufuna kupusher whip
See me on TV (TV) musandisowe kwambiri (kwambiri)
Utha kutenga pic tikakumana mu street (mu street)
Ndikupanga izizi chifukwa fanz ndimakukondani
[Chorus: Kushizzo & Nkhiwa]
Pepani nakusiyani mukudikira (mukudikira)
Koma tape ina nditulutsa mu July (mu July)
Ndili mu stu nyimbo ndikujudula (kujudula)
Kudya ma beat ngati ndikufutula (futula aah)
Kufuna ndizikuona ukumwetulira (mwetulira aah)
Uzindiwuza ndizipanga Mene ukufunira (ukufunira aah)
Osandinyoza lero moyo ndiwozungulira (ndiwozungulira aah)
Uzandipeza pompa ukazungulira (ukazungulira)
Pepani nakusiyani mukudikira (mukudikira)
Koma tape ina nditulutsa mu July (mu July)
Ndili mu stu nyimbo ndikujudula (kujudula aah)
Kudya ma beat ngati ndikufutula (futula aah)
Kufuna ndizikuona ukumwetulira (mwetulira aah) (It's Prodogy)
Uzindiwuza ndizipanga Mene ukufunira (ukufunira aah)
Osandinyoza pano moyo ndiwozungulira (ndiwozungulira aah)
Uzandipeza pompa ukazungulira (ukazungulira)