Waganiza Bwanji by Jeff Nyimbo (Ft. Brainlock Kushizzo)
Waganiza Bwanji by Jeff Nyimbo (Ft. Brainlock Kushizzo)

Waganiza Bwanji

Jeff Nyimbo & Kushizzo * Track #2 On Songs Of Solomoni

The music player is only available for users with at least 1,000 points.

Download "Waganiza Bwanji"

Waganiza Bwanji by Jeff Nyimbo (Ft. Brainlock Kushizzo)

Release Date
Fri Dec 29 2023
Performed by
Jeff NyimboKushizzo
Produced by
Nkhiwa
Writed by
Kushizzo & Jeff Nyimbo & Nkhiwa

Waganiza Bwanji Lyrics

[Intro: Jeff Nyimbo]
It's you that Mega
Okay

[Chorus : Jeff Nyimbo & Kushizzo]
Waganiza bwanji? Waganiza chani?
Umapanga chan?i izi wapangiranji?
Ubwelera mbuyo kapena uzingopitabe
Ukhala pomwepa kapena ufuna usunthe?
Waganiza bwanji? Waganiza chani?
Umapanga chan?i izi wapangiranji?
Ubwelera mbuyo kapena uzingopitabe (Kushizzo)
Ukhala pomwepa kapena ufuna usunthe?

[Verse 1 : Kushizzo]
Don't stop living your life
Tsogolo lili manja mwako uzikumbukira
Upeze njira uthane nazo zikachuluka
Usasiyile panjira wachoka kutali kumbuka,utanyamuka
Unali ndi lotto limodzi ,kudzayangalira ma sister ndima Bro's
Koma apa lero kusintha iwe ndi chani Kodi?
Kuyiwala zomwe timakambirana limodzi
Choice ndi yako uzivaya kapena uyima pompa
Wagwa pansi koma dzuka kakamira loto
Moyo ndi kamodzi panga ganizo la bho
Utha kuseka lero koma uzalira mtsogolo

[Chorus : Jeff Nyimbo]
Waganiza bwanji? Waganiza chani?
Umapanga chan?i izi wapangiranji?
Ubwelera mbuyo kapena uzingopitabe
Ukhala pomwepa kapena ufuna usunthe?
Waganiza bwanji? Waganiza chani?
Umapanga chan?i izi wapangiranji?
Ubwelera mbuyo kapena uzingopitabe
Ukhala pomwepa kapena ufuna usunthe?

[Verse 2: Jeff Nyimbo]
Moyo ndiwophwеka umangofuna plan
Ukadzadza denga uli ndi ukali
Plan plan ndi plan osayisintha man
Mkazi ndi mkazi amasintha man
Analipa nzako anagwetsedwa
Analipa pa nzako anachеperapo
Ukhoza kukhala dolo koma usali dolo
Usadikire kuti zikupeze pa mkono
Uzizite wasnga bwino paliponse liwiro
Kumakhala ndi nkhwiro kusaka Kuli mpoto
Kuti uchiphule kuchichotsa pa Moto
Kumalingalira patali tikuvaya konko

[Chorus : Jeff Nyimbo]
Waganiza bwanji? Waganiza chani?
Umapanga chan?i izi wapangiranji?
Ubwelera mbuyo kapena uzingopitabe
Ukhala pomwepa kapena ufuna usunthe? (It's you that Mega)
Waganiza bwanji? Waganiza chani?
Umapanga chan?i izi wapangiranji?
Ubwelera mbuyo kapena uzingopitabe
Ukhala pomwepa kapena ufuna usunthe?

Waganiza Bwanji Q&A

Who wrote Waganiza Bwanji's ?

Waganiza Bwanji was written by Kushizzo & Jeff Nyimbo & Nkhiwa.

Who produced Waganiza Bwanji's ?

Waganiza Bwanji was produced by Nkhiwa.

When did Jeff Nyimbo release Waganiza Bwanji?

Jeff Nyimbo released Waganiza Bwanji on Fri Dec 29 2023.

Your Gateway to High-Quality MP3, FLAC and Lyrics
DownloadMP3FLAC.com