Bwinobwino by Jeff Nyimbo
Bwinobwino by Jeff Nyimbo

Bwinobwino

Jeff Nyimbo * Track #12 On Songs Of Solomoni

The music player is only available for users with at least 1,000 points.

Download "Bwinobwino"

Bwinobwino by Jeff Nyimbo

Release Date
Fri Dec 29 2023
Performed by
Jeff Nyimbo
Produced by
Nkhiwa
Writed by
Jeff Nyimbo & Nkhiwa

Bwinobwino Lyrics

[Intro]
It's You That Mega

[Chorus]
Ndili bwinobwino ndilibwinobwino
Ukapweketsa ine uchotsedwa dzino
Ndikupanga dzina dollar kupanga zina
Mkazi akatripa tikupeza wina

[Hook]
Ndili bwinobwino ndilibwinobwino
Ndili bwinobwino ndilibwinobwino

[Verse]
Ndili bhobho mongasukuwona wekha
Tili pompa sitikupita komwe kwa tentha
Ukayishosha dziwa kuti sindikubwera ndekha
Ukayipa dziwa Nyimbo
Chi mfana chaku mpanda pa mpanda Ku 49
After kubanda tukadya chiwaya mu Guliver
Tsogolo kuwala kwambiri mafana sakutayima
Sindikuyankha ndili busy mwina yesa Ku Typer
Beast pa beat nde ndikubwera ndi yokalipa
Ndamuvula beat ukudziwa masiku omaliza
Amazimva u Gee koma akayamba sakumaliza
Moto ndi unadi mukafuna mutha kupaliza
Fresh to death ndakumana ndichi Richmond
Face To face sungalimbane ndi ine
Ase Ndili bwinobwino mu dancehall Ase
Sitilimodzi koma basi kubwata koma ase

[Chorus]
Ndili bwinobwino ndilibwinobwino
Ukapweketsa ine uchotsedwa dzino
Ndikupanga dzina dollar kupanga zina
Mkazi akatripa tikupeza wina

[Hook]
Ndili bwinobwino ndilibwinobwino
Ndili bwinobwino ndilibwinobwino
It's You That Mega

Bwinobwino Q&A

Who wrote Bwinobwino's ?

Bwinobwino was written by Jeff Nyimbo & Nkhiwa.

Who produced Bwinobwino's ?

Bwinobwino was produced by Nkhiwa.

When did Jeff Nyimbo release Bwinobwino?

Jeff Nyimbo released Bwinobwino on Fri Dec 29 2023.

Your Gateway to High-Quality MP3, FLAC and Lyrics
DownloadMP3FLAC.com