Usandipope by Dirty Flo (Ft. Crispy Malawi)
Usandipope by Dirty Flo (Ft. Crispy Malawi)

Usandipope

Dirty Flo & Crispy Malawi * Track #8 On CHINDUNJI LONG PLAY

The music player is only available for users with at least 1,000 points.

Download "Usandipope"

Usandipope by Dirty Flo (Ft. Crispy Malawi)

Performed by
Dirty FloCrispy Malawi
Produced by
F9INE (MWI)
Writed by
Dirty Flo & Crispy Malawi & F9INE (MWI)

Usandipope Lyrics

[Intro : Dirty Flo & Crispy Malawi]
F9INE Entertainment
Brr! Gang, Gang, Gang, Gang, Gang
Yoh Dirty, Dirty, Dirty
Yeah Spe, Spe, Spe

[Verse 1: Dirty Flo & Crispy Malawi]
Kufika kupanga attack ndi defence (Ma Dolo!)
The fans say I drive her crazy, ali Ku chiphedi
Ma Jam Alipo kale tungosaka bread
Jah, Jah waflippa ma odds, hater waluza bet

[Chorus: Crispy Malawi & Dirty Flo]
Usandipope choncho ndisazimve (Mmh hm)
Ngati zisali za ndalama ndisazimve (Ayi)
Kuzipereka ndi uku koma sindingagive (No way)
Zimangofunika Ku wekha ndi khalidwe (Khalidwe)
Yeah
Usandipope choncho ndisazimve(no, nooo)
Ngati zisali za ndalama ndisazimve
Kuzipereka ndikokoma sindingagive (No way)
Zimangofunika Ku wekha ndi khalidwe (Khalidwe)

[Verse 2: Crispy Malawi & Dirty Flo]
Don't tell me what to do (To do)
Ndili ndi Dirty, Hater ndikuthila doom (Fefe)
Ndili mu zone, ndayika basket (Zone) (Basket)
Ndimapusha ngati ndine advert (Advert)
I got the juice ngati nanchesi (Juice, Juice)
Ku runner dancehall ngati athlete
Takudutsa ngati passage
Tungosakaso Zi money
Kufuna Ku baller ndi A'bale
Nane I got goals, ndeno sindingakuseve
Yeah I look alive komano ndafa ndiphwete (Hahaha)
Ndingo chiller ndi ziwindi ndili mkati chani
Mfana woti ndinavaya osakutsanzikani
Nde Ka landlord kanu kaja kamati chani?
Super glue with the game mati mati chani?
Ndinaba game fukwa ndinalibe game
Ndili youngin
Mfana sangandigunde pss, I left them hangin'

[Chorus: Crispy Malawi & Dirty Flo]
Usandipope choncho ndisazimve (Ooh oh)
Ngati zisali za ndalama ndisazimve (Ndisazimve) (Uh)
Kuzipereka ndikokoma sindingagive (No, No)
Zimangofunika Ku wekha ndi khalidwe (Khalidwe)
Usandipope choncho ndisazimve (Ndisazimve)
Ngati zisali za ndalama ndisazimve (Ndisazimve)
Kuzipereka ndikokoma sindingagive (Uh, huh)
Zimangofunika Ku wekha ndi khalidwe (Eeh, eeh)

[Outro: Dirty Flo]
Uh, huh, huh, uh, huh, uh, huh
Uh, huh, huh,uh, huh, uh, huh

Usandipope Q&A

Who wrote Usandipope's ?

Usandipope was written by Dirty Flo & Crispy Malawi & F9INE (MWI).

Who produced Usandipope's ?

Usandipope was produced by F9INE (MWI).

Your Gateway to High-Quality MP3, FLAC and Lyrics
DownloadMP3FLAC.com