[Intro]
F9INE Entertainment
Yeah
Yea, yea, yea
Timothy Got the fire beats no matter what it is
Yeah, yeah, yeah, yeah
(Yea, yea, yea, yea)
[Chorus]
Njala ya ndi pinda (yea)
Ndadya ma indica (yea)
Ndadula phone bwa? (Bwa)
Huh I'm in the cut
Ndafatsa kukupeza, Nkhawa yandipeza (peza)
Mutu kuvomera, Mtima wandiletsa (wandiletsa)
Huh yea
Njanja (Njanja) iwe saletsa
Njanja (Njanja) iwe saletsa
Njanja (Njanja) iwe saletsa
Huh, huh, Njanja ,Njanja (Njanja) iwe saletsa
Njanja (Njanja) iwe saletsa
Njanja (Njanja) iwe saletsa
[Verse 1]
Mengalenga ana a Mlengi tungoyamika[?]
Kuphula sin osawopa zoti lil Bro akanena
Za ine ndiye mwanenadi
Koma zanu hmm, hmm sindinamve (Yea)
Ndine mfana ofewa angofuna kulimbana nane (hmm)
I ain't falling for no hoe ndiziwankhe (mmh mh)
Moni ndi ulere koma ndafunsa zikuti bwanji? Yeah (Mmh)
Ngati dollar sikukwana ndeti nzako akuyankhire
Ati sindingasiye Ku dropper ma hit
That's why they love me alot
But I'mma need more than that
Pano si mwayi ndaneneratu [?]
Yeah,Titha kunjanja limodzi osapondana phazi
Yeah,Mkazi ukunjanja nayeso kukana pansi (yeah)
Baddie kupota baddie (baddie)
Ndiphaka onse koma ndifunabe phaxi
[Chorus]
(Fukwa) Njala ya ndi pinda (yea)
Ndadya ma indica (yea)
Ndadula phone bwa? (Bwa)
Huh I'm in the cut
Ndafatsa kukupeza, Nkhawa yandipeza
Mutu kuvomera, Mtima wandiletsa
Huh yea
Njanja (Njanja) iwe saletsa
Njanja (Njanja) iwe saletsa
Njanja (Njanja) iwe saletsa
Huh, huh, Njanja ,Njanja (Njanja) iwe saletsa
Njanja (Njanja) iwe saletsa
Njanja (Njanja) iwe saletsa
[Verse 2]
(Kudyerera)
Kudyerarera
Got high high kandilemba
Most High analemba
Mfana zatentha (zatentha)
Yeah
Nkhani ya moni pa mbali pa
Sindingakuopeni mafana (No) mwandipeza
Jah Jah wadalitsa (yea)
Njanja iwe yamika
Mphasa akazima
Mmh Rasta wamaliza
[Outro]
Timothy Got the fire beats no matter what it is
Saletsa was written by Dirty Flo & F9INE (MWI) & Timothy Got The Fire Beats No Matter What It Is.
Saletsa was produced by F9INE (MWI) & Timothy Got The Fire Beats No Matter What It Is.