[Intro]
Aseh Gwamba, uli kutiko?
Mm, nduvaya ku church aseh
Iyayi panopa ta-caller zima-chick aseh, kuli zima-chick zinazake six
Iyayi man nduvaya ku church aseh
Four zaku [?], two zaku DMI
Ndagula nkunda [?]
Ih, lero ndi Friday nde timavaya ku church aseh
Inunso amwene
Sungamvetsetse
[Verse 1]
Unali kale iwe, uli ndi ma chick ten
Amachita kukumana kupatsana ma turn
Lero kubwera Mary mawa kubwera Jane
Pakamwa pako nthawi zonse Mary Jane
Pano kuku-caller Friday uli ku church
Team yamadolo mphwanga uli pa bench
Iwe kumapemphera ife tikuwupeza
Man Gwamba anakupusitsani Major
Timamenya drug, timamenya bag
Maluzi kubwera iwe kupinyulitsa shirt
Nthawi zina akabwera kupinyulitsa ka key
Umakonda ma bomba timakutcha Iraq
[Chorus]
Unali kale iwe!
(Pano suzitsata, tikamenya beef nanga bwanji sutiyankha?)
Ha, unali kale iwe!
(Pano suli gutter, ukuyimba zotukwana muja unkatiwaza)
Gwamba, unali kale iwe!
(Pano suzitsata, tikamenya beef nanga bwanji sutiyankha?)
Unali kale iwe!
(Pano suli gutter, ukuyimba zotukwana muja unkatiwaza)
[Verse 2]
Nde man Gwamba simubwera, eh?
Ee aseh damani
Zomwe mupangazo ndinapanga kukuposani
Ndikuziwa bwino moyo msapange makani
Kuzitchela nokha mawali muli pa mpani
Man zimenezo m'mapindula chani?
Kuwononga dollar, kufuna ku baller
Kufuna kugula phax, mnthumba osalola
Mwazuka ndi Flora komano ndi mbola
Chifukwa aliyense ali ndi dollar amamu-caller
Komano man ndinu friend osamakhala chonchi
Mumuyese Yesu Christu otifela pa cross
Mukapeza nthawi mutipezeko ku temple
Mawu a Namalenga aja muzawamveko
[Outro]
Unali kale iwe!
Ha, unali kale iwe!
Gwamba, unali kale iwe!
Eh? Unali kale iwe!
Eh? Unali kale iwe!
Unatha
Unatha
Unatha
(Ayi, ayi, ayi, ayi, ayi, ayeye)
Unatha
Unatha
(Ayi, ayi, ayi, ayi, ayi, ayeye)
(Ayi, ayi, ayi, ayi, ayi, ayeye)
(Ayi, ayi, ayi, ayi, ayi, ayeye)
Unatha