[Chorus: Nimix]
Mm, yeah
King of kings
Lord of lords
Great provider, the master of all (Oya-oya-oya)
King of kings
Lord of lords
Great provider, the master of all
Oba, Oba (Yeah-yeah)
Oba, Oba (Lala-lali, lala-lala)
Oba, Oba
Oba, Oba (Oh, nana-nana, nana-nana)
[Verse 1: Gwamba]
Aish, ndikakuwona komwe ndikuchoka
Ndikutali komwe mwandichotsa
Ndikamayenda slow kundikoka
Madalitso tola four ngati joker
Sindikuchoka
Madalitso kupeleka chikoka
Anthu onse omwe amanyoza
Sindinatalky adzapepesa okha
Mbuye podalitsa munthu amangodalitsa sapanga consult
Zosatheka zija pano zatheka amvekele illuminati
[Chorus: Nimix]
Oba, Oba (Yeah-yeah)
Oba, Oba (Lala-lali, lala-lala)
Oba, Oba
Oba, Oba (Tonight I praise, tonight I praise [?])
[Verse 2: Tay Grin]
He's king I'm his servant
All this drip, profits from serving
None o' my biz but you can profit if you believe in the almighty
Almighty father we here
Everytime I pray to you things get clearer
You're my backbone
You're my shelter
When trouble come me na fear
Olo atabwera dyabulosi
Ndidzamuwuza zakukhosi
Ine ndine mwana wa Jehova
Ine toto babiloni
[Chorus: Nimix]
Oba, Oba (Yeah-yeah)
Oba, Oba (Lala-lali, lala-lala)
Oba, Oba
Oba, Oba (Oh, nana-nana, nana-nana)
[Verse 2: Gwamba]
Eh, mbuye wanga ndikuwopa
Padziko pa pachuluka njoka
Moyo wanga uli mwa inu nokha
Ndudziwa simungandisiye pompa, huh
Simunathane nane
Kuli konse ndingapite muli nane
Ndine msilikali wa Yesu, ukandifuna undipeza mu army
Mbuye podalitsa munthu amangodalitsa sapanga consult
Zosatheka zija pano zatheka amvekele illuminati
[Chorus: Nimix]
Oba, Oba (Yeah-yeah)
Oba, Oba (Lala-lali, lala-lala)
Oba, Oba
Oba, Oba (Oh, nana-nana, nana-nana)