Samayankha by KwemoGoon
Samayankha by KwemoGoon

Samayankha

KwemoGoon * Track #3 On New Wave No Cap (EP)

The music player is only available for users with at least 1,000 points.

Download "Samayankha"

Samayankha by KwemoGoon

Release Date
Mon Aug 17 2020
Performed by
KwemoGoon
Produced by
KwemoGoon 265 Records
Writed by
Ibrahim KwemoGoon Abdul

Samayankha Lyrics

[Intro]
Yeah
Yahh, ahh
(DaVinci)
Ahh, ahh
Yeah

[Chorus]
Ndikayimba phone imangoti busy
Mwina anandiyika blacklist, andiuze
Mwina unandiblocker, chifukwa sumayankha
Mwina zinakubhowa zimene ndinapanga
Kutumiza ka text, samayankha
Olo kuvunga ka VN, samayankha
Kumenya video call, samayankha
Olo iweyo umu beepe, samayankha, yah

[Verse 1]
Chama nine, kalowano online
Ine pompopompo 'Hie' , koma no reply men
Maybe she got pride or maybe she don't do love
Sikayankha ayi, kaya nchani kamafuna
Komabe sindiyiva, inebe ndihalabe
Ndizingo beeper olo usandiyankhe
I just want to talk, koma iweyo you don't want to
Umangodusa ngati sumaziwa kwathu

[Refrain]
Give me a chance, yeah
Ndipase mwayi
Mwina ndi ineyo amene mangokutayitsa zinthawi
Give me a chance, yeah
Ndipase mwayi
Mwina ndi ineyo amene mangokutayitsa zinthawi

[Chorus]
Ndikayimba phone imangoti busy
Mwina anandiyika blacklist, andiuze
Mwina unandiblocker, chifukwa sumayankha
Mwina zinakubhowa zimene ndinapanga
Kutumiza ka text, samayankha
Olo kuvunga ka VN, samayankha
Kumenya video call, samayankha
Olo iweyo umu beepe, samayankha

[Verse 2]
Maybe 'cause I'm broke, koma uziyankhako bho
Kuyesa kumenya call, koma you don't pick up no
Koma number yako aise unandipatsa wekha
Mwina azinzako anakutalker kuti sindiworker
What's the problem? tandiuze
Mwina vuto ndine, tandiuze
Koma dekha, sine opusa
Ndangofusa chifukwa zimandizuza ine

[Refrain]
Give me a chance, yeah
Ndipase mwayi
Mwina ndi ineyo amene mangokutayitsa zinthawi
Give me a chance, yeah
Ndipase mwayi
Mwina ndi ineyo amene mangokutayitsa zinthawi

[Chorus]
Ndikayimba phone imangoti busy
Mwina anandiyika blacklist, andiuze
Mwina unandiblocker, chifukwa sumayankha
Mwina zinakubhowa zimene ndinapanga
Kutumiza ka text, samayankha
Olo kuvunga ka VN, samayankha
Kumenya video call, samayankha
Olo iweyo umu beepe, samayankha

[Outro]
(DaVinci)
Samayankha
Samayankha
Samayankha
Samayankha

Samayankha Q&A

Who wrote Samayankha's ?

Samayankha was written by Ibrahim KwemoGoon Abdul.

Who produced Samayankha's ?

Samayankha was produced by KwemoGoon 265 Records.

When did KwemoGoon release Samayankha?

KwemoGoon released Samayankha on Mon Aug 17 2020.

Your Gateway to High-Quality MP3, FLAC and Lyrics
DownloadMP3FLAC.com