Promise by KwemoGoon
Promise by KwemoGoon

Promise

KwemoGoon * Track #2 On New Wave No Cap (EP)

The music player is only available for users with at least 1,000 points.

Download "Promise"

Promise by KwemoGoon

Performed by
KwemoGoon

Promise Lyrics

[Intro]
[?]

[Chorus]
Ndisanakukonde darlie ndiwuze kaye
Kuti you really down for me
You go ride or die
Olo nsaku worker iwe suzandithawa?
Mwina ukonda fame, ndilole ndizivaya
Promise me you won't go
Kundisiya, kundithawa, kukagwidwa ndi ntchana
Promise me you won't go
Oh-ooh-oh, oh no
You won't go

[Verse 1]
Mwina wangolola chifukwa uli desperate
Tell me mwina ufuna kuwawitsa Ex
Ih ih, mwina sinzapusha ine
Gist mwina sinzaphula ine
Kuthobwera Gwamba, Macelba ndi Gamba
Zidollar kukublesser ku Airtel Money, Mpamba
Kuthobwera Rich, Versace Nekhai
Ndeuti wangotchena asie wangowubaya
Kutabwera Kell Kay, are you gon' stay?
Olo uzandikana, are you gon' runaway?
Kutabwera Dettе ndi hit undikakamile
Suzandithawa kukagwidwa ndiye?

[Refrain]
Nanga anawa uzawasamala?
Olo kwina uzakakwatira?
Nanga anawa uzawasamala?
Olo kwina uzakakwatira?

[Chorus]
Ndisanakukonde darliе ndiwuze kaye
Kuti you really down for me
You go ride or die
Olo nsaku worker iwe suzandithawa?
Mwina ukonda fame, ndilole ndizivaya
Promise me you won't go
Kundisiya, kundithawa, kukagwidwa ndi ntchana
Promise me you won't go
Oh-ooh-oh, oh no
You won't go

[Verse 2]
Kuthobwera VC, suzavera ma friends?
Kundisiya kukagwidwa ndi Neezh
Kuthobwera Shmurda mbali atameta
Atangotchena, spray akumveka
Nanga kutabwera azibusa aja
Che Wikise ndi Conqueror
Suzabwera ndi pompaja? kundisiya ndikundithawa
Nanga zitavuta ngini osapusha
Ndiuziletu uzandisamala
Nanga zitavuta mavuto kuchuluka
Ndiuziletu uzandithangata

[Refrain]
Nanga anawa uzawasamala?
Olo kwina uzakakwatira?
Nanga anawa uzawasamala?
Olo kwina uzakakwatira?

[Chorus]
Ndisanakukonde darlie ndiwuze kaye
Kuti you really down for me
You go ride or die
Olo nsaku worker iwe suzandithawa?
Mwina ukonda fame, ndilole ndizivaya
Promise me you won't go
Kundisiya, kundithawa, kukagwidwa ndi ntchana
Promise me you won't go
Oh-ooh-oh, oh no
You won't go

Your Gateway to High-Quality MP3, FLAC and Lyrics
DownloadMP3FLAC.com