Ndalama Remix by Trappy Beats,Quest (MW),Zeze Kingston
The music player is only available for users with at least 1,000 points.

Download "Ndalama Remix"

Ndalama Remix by Trappy Beats,Quest (MW),Zeze Kingston

Release Date
Sun May 22 2022
Produced by
Trappybeats.
Writed by
Trappybeats. & Quest (MWI) & Zeze Kingston

Ndalama Remix Lyrics

[Intro]
Aseh Trappy!

[Chorus :Trappy Beats]
Ndakuthela Ma Plan (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?)
Kodi Nnalakwa Chani? (Kuchulusa) (Kuchulusa) (Kuchulusa)
Miseche Ndizi Nkhani (Chifukwa Cha) (Chifukwa Cha!) (Chifukwa Cha!)
Ndalama Ndalama (Aah aah ah)

[Verse 1:Quest]
Mpaka akudana nane akuyesa ndili ndi ndalama
Man muzingo hasser hasser basi
Nkhani nde ndikungoyika calm
Mene ndikuspendela sindingakuwuze
Mene tukazisaka sindinakuwuze
Ngati ulibe sungandiuze
Ndi kale ndinadandaula kuti life ikuyenda Slow-Mo
Ine ayi ndili mkati momo
Because I be spending like Jomo
Ndalama ndi nsamo
Olo andinyoze, andikambe, andiseke ine vibe ndi hundrede
Olo andihate ine chete ma plan agona pa mandede

[Chorus: Trappy Beats & Zeze Kingston]
Ndakuthela Ma Plan (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?)
Kodi Nnalakwa Chani? (Kuchulusa) (Kuchulusa) (Kuchulusa)
Miseche Ndizi Nkhani (Chifukwa Cha) (Chifukwa Cha!) (Chifukwa Cha!)
Ndalama Ndalama (Aah aah ah)
Ndakuthela Ma Plan (Ndipange Bwanji?) (Ma plan) (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?)
Kodi Nnalakwa Chani? (Kuchulusa) (Kuchulusa) (Kuchulusa)
Miseche Ndizi Nkhani (Ayo Trappy!, Tiyeni!)(Chifukwa Cha) (Chifukwa Cha!) (Chifukwa Cha!)
Ndalama Ndalama (Tiyeni!, Tiyen!,Tiyeni! eish!)
Ndalama Ndalama (Aah aah ah)

[Verse 2: Zeze Kingston]
Zibwana ndimapanga (Zibwana ndimapanga)
Posaka ndalama (Posaka ndalama)
Zibwana sitipanga (Zibwana Sitipanga)
Posaka ndalama (Posaka ndalama)
Ndiye ndiwe ndani? umatani?
Usandipatse busy
Dzina ndani? umatani?
Usandipatse busy
Ndiwe ndani? umatani?
Usandipatse busy
Dzina ndani? umatani?
Usatipatse busy
Eish!

[Bridge: Trappy Beats & Zeze Kingston]
Maluzi Maluzi Maluzi
Maluzi Maluzi Maluzi (Musiye Mzako)
Maluzi Maluzi Maluzi
Maluzi Maluzi Maluzi (ooh Musiye Mzako) (M'siye Nzako)
Maluzi Maluzi Maluzi
Maluzi Maluzi Maluzi (Musiye Mzako) (Eish!!)
M'siye Nzako
Maluzi Maluzi Maluzi
Maluzi Maluzi Maluzi
M'siye Nzako

[Pre-Chorus :Trappy Beats]
Ndakuthela Ma Plan(Maluzi Maluzi Maluzi)(Maluzi Maluzi Maluzi)
Kodi Nnalakwa Chani (Maluzi Maluzi Maluzi) (Maluzi Maluzi Maluzi) (M'siye Nzako)
Ndakuthela Ma Plan (Maluzi Maluzi Maluzi) (Maluzi Maluzi Maluzi)
Kodi Nnalakwa Chani (Maluzi Maluzi Maluzi) (Maluzi Maluzi Maluzi) (M'siye Nzako)
Ndalama Ndalama
Maluzi Maluzi Maluzi M'siye Nzako

[Chorus: Trappy Beats]
Ndakuthela Ma Plan (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?)
Kodi Nnalakwa Chani? (Kuchulusa) (Kuchulusa) (Kuchulusa)
Miseche Ndizi Nkhani (Chifukwa Cha) (Chifukwa Cha!) (Chifukwa Cha!)
Ndalama Ndalama (Aah aah ah)
Ndakuthela Ma Plan (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?)
Kodi Nnalakwa Chani? (Kuchulusa) (Kuchulusa) (Kuchulusa)
Miseche Ndizi Nkhani (Chifukwa Cha) (Chifukwa Cha!) (Chifukwa Cha!)
Ndalama Ndalama (Aah aah ah)

Ndalama Remix Q&A

Who wrote Ndalama Remix's ?

Ndalama Remix was written by Trappybeats. & Quest (MWI) & Zeze Kingston.

Who produced Ndalama Remix's ?

Ndalama Remix was produced by Trappybeats..

When did Trappy Beats,Quest (MW),Zeze Kingston release Ndalama Remix?

Trappy Beats,Quest (MW),Zeze Kingston released Ndalama Remix on Sun May 22 2022.

Your Gateway to High-Quality MP3, FLAC and Lyrics
DownloadMP3FLAC.com