Ndalama by Trappy Beats
The music player is only available for users with at least 1,000 points.

Ndalama Lyrics

[Chorus]
Aseh Trappy!
Ndakuthela Ma Plan (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?)
Kodi Nnalakwa Chani? (Kuchulusa) (Kuchulusa) (Kuchulusa)
Miseche Ndi zi Nkhani (Chifukwa Cha) (Chifukwa Cha!) (Chifukwa Cha!)
Ndalama Ndalama (Aah aah ah)

[Verse 1]
Maluzi Ndatchekela
Ulimi Nnayesa Kale
Ku runner ma taxi
Kuna ma tip
Kusaka money tiguleko drip
Ndalama Ndalama Ndalama Ndalama Satana
Ndalama Ndalama Ndalama Ndalama Satana
Kudzuka mma three ku den pita mma ten
Osagona kusaka ma change
Kudzuka mma three ku den pita mma ten
Osagona kusaka ma change
Ndaleka ndaleka zibwanazo ndaleka
Ndatopa Ndatopa Eh Zandicheka cheka

[Chorus]
Ndakuthela Ma Plan (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?)
Kodi Nnalakwa Chani? (Kuchulusa) (Kuchulusa) (Kuchulusa)
Miseche Ndi zi Nkhani (Chifukwa Cha) (Chifukwa Cha!) (Chifukwa Cha!)
Ndalama Ndalama (Aah aah ah)

Ndakuthela Ma Plan (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?)
Kodi Nnalakwa Chani? (Kuchulusa) (Kuchulusa) (Kuchulusa)
Misechе Ndi zi Nkhani (Chifukwa Cha) (Chifukwa Cha!) (Chifukwa Cha!)
Ndalama Ndalama (Aah aah ah)

[Verse 2]
Yah yah
Nkhani ndikunvana
Nkumasaka Ndalama yah yah
Mpakana Kudana Kamba ka ndalama yah yah
Nkhani Ndikunvana
Nkumasaka Ndalama yah yah
Yah yah
Yah yah
Maluzi Maine
Wandisiya Mmalere
Usandiuzе Maine
Ndikungosaka Mandede
Ndaleka ndaleka zibwanazo ndaleka
Ndatopa Ndatopa Eh Zandicheka cheka

[Bridge]
Maluzi Maluzi Maluzi
Maluzi Maluzi Maluzi
Maluzi Maluzi Maluzi
Maluzi Maluzi Maluzi
M'siye Nzako
Maluzi Maluzi Maluzi
Maluzi Maluzi Maluzi
M'siye Nzako

[Pre-Chorus]
Ndakuthela Ma Plan(Maluzi Maluzi Maluzi)(Maluzi Maluzi Maluzi)
Kodi Nnalakwa Chani (Maluzi Maluzi Maluzi) (Maluzi Maluzi Maluzi)

Ndakuthela Ma Plan (Maluzi Maluzi Maluzi) (Maluzi Maluzi Maluzi)
Kodi Nnalakwa Chani (Maluzi Maluzi Maluzi) (Maluzi Maluzi Maluzi)
Ndalama Ndalama

[Chorus]
Ndakuthela Ma Plan (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?)
Kodi Nnalakwa Chani? (Kuchulusa) (Kuchulusa) (Kuchulusa)
Miseche Ndi zi Nkhani (Chifukwa Cha) (Chifukwa Cha!) (Chifukwa Cha!)
Ndalama Ndalama (Aah aah ah)

Ndakuthela Ma Plan (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?) (Ndipange Bwanji?)
Kodi Nnalakwa Chani? (Kuchulusa) (Kuchulusa) (Kuchulusa)
Miseche Ndi zi Nkhani (Chifukwa Cha) (Chifukwa Cha!) (Chifukwa Cha!)
Ndalama Ndalama (Aah aah ah)

Ndalama Q&A

Who wrote Ndalama's ?

Ndalama was written by Trappybeats..

Who produced Ndalama's ?

Ndalama was produced by Trappybeats..

When did Trappybeats. release Ndalama?

Trappybeats. released Ndalama on Tue May 23 2023.

Your Gateway to High-Quality MP3, FLAC and Lyrics
DownloadMP3FLAC.com