M'manja by Brainlock T-Kas & Nkhiwa
The music player is only available for users with at least 1,000 points.

M’manja Lyrics

[Chorus: Nkhiwa]
It's you that Mega
Ma trapper ndi ife tikafika mutiwombele M'manja
Smokes ndiyambiri timagawiza ndi a gover
Ndikungo sipper Zi syrup
Oooh ooh
Ndikungo Zi syrup
Imma focus on her cuz Imma keep her (imma keep her)
Azibale anga imma keeper (imma keep her)
It's a real star shining in the dark (darrkkk)
Ndikuwona chifukwa cha mdima[?]
Ukufuna kundiona ngati kanema
Sindikudikira iyi ndi meme[?]
Ndikungosewera moyo ndi game
Ukumva kuwawa usati blame

[Verse 1: Nkhiwa]
Yeah yeah
Kudabwa Nkhiwa wafika pamalo
M'manja Muli chi double cup (double)
What you trappin baby girl for my mum[?]
Free Jeffrey yeah spider (slatt)
Chasing the money tryna[?]
Recycle me like a plastic paper
I've been making money with my gang
I don't stop
Ukufuna ng'ongole bwelеtsa collateral
Ooh ooh
I take care of family and friеnds
Yeah
You ou
Osa waster yanga time
Chifukwa I'm pa news[?]
Yeah
Zikamayenda kufuna kundiyika pansi
Yeah yeah
Trap ndi yomwe ija I can see them stars[?] (see the stars)
Pressure pressure I turn it into diamonds [?]
Tikungo kweza level
We'll be burning the stash
Yeaaah yeah

[Bridge: Brainlock T-Kas]
In just winning
I'm just coming
Told the doctor I'm just drowning
Yeah you may drip or drown
Yeaaah yeahhh
Im just winning
I'm just coming
Told the doctor I'm just drowning
Yeah you may drip or drown
Yeaaah yeahhh

[Chorus: Nkhiwa]
Ma trapper ndife tikafika mutiwombele M'manja
Smokes ndiyambiri timagawiza ndi a gover
Ndikungo sipper Zi syrup
Ndikungo Zi syrup
Imma focus on her cuz I'm a keep her
Azibale anga imma keeper
It's a real star shining in the dark
Ndikuwona chifukwa cha mdima[?]
Ukufuna kundiona ngati kanema
Sindikudikira iyi ndi meme[?]
Ndikungosewera moyo ndi game
Ukumva kuwawa usati blame

[Verse 2: Brainlock T-Kas]
Umvestele ulemere ukhale mkati
Akakukoka usalore iwe ndiwamakani
Ali m'maso Akufuna nkhani[?]
Ukakhala ulipa bho amafuna kuti akuyikepansi
Trap ndi yomwe ija anasintha ndi ma style
Themba ndi yemwe Uja
Akungo tamangitsa ma file
Abale okondedwa ndi amene ndili nawo
Ndikafika pa spot amafuna[?]
[?] Nde wakoma nkhope yanga yonona
Lero sitikugona lero tichipota
Life inasintha pano sindimamwa mowa
I told [?] My time
Munkayesa ndi mabodza
Family first imma keeper
The strap on me imma keep it
Phone be out don't reach me
Don't call me I'm in a meeting
[?]
Ndachoka patali I mean it
All I had is one minute
Now I got the cops in my business

[Chorus: Nkhiwa]
Ma trapper ndife tikafika mutiwombele M'manja
Smokes ndiyambiri timagawiza ndi a gover
Ndikungo sipper Zi syrup
Ndikungo Zi syrup
Imma focus on her cuz I'm a keep her
Azibale anga imma keeper
It's a real star shining in the dark
Ndikuwona chifukwa cha mdima[?]
Ukufuna kundiona ngati kanema
Sindikudikira iyi ndi meme[?]
Ndikungosewera moyo ndi game
Ukumva kuwawa It's you that Mega usati blame

M’manja Q&A

Who wrote M’manja's ?

M’manja was written by Brainlock T-Kas & Nkhiwa.

Who produced M’manja's ?

M’manja was produced by Nkhiwa.

When did Brainlock T-Kas & Nkhiwa release M’manja?

Brainlock T-Kas & Nkhiwa released M’manja on Fri Nov 03 2023.

Your Gateway to High-Quality MP3, FLAC and Lyrics
DownloadMP3FLAC.com