Themba ndi Themba by Brainlock T-Kas & Nkhiwa
Themba ndi Themba by Brainlock T-Kas & Nkhiwa

Themba ndi Themba

Brainlock T-Kas & Nkhiwa * Track #1 On Themba Ndi Themba

The music player is only available for users with at least 1,000 points.

Themba ndi Themba Lyrics

[Intro: Nkhiwa]
Yeah
Themba Themba Themba
Themba Themba Themba
Themba
Themba

[Chorus : Brainlock T-Kas]
Amayesa kuti ifeyo ndi mphwemphwa
Anangodabwa ndangofika ndikubhebha
Trap yathu sungalowe chifukwa siwe member
Iyi ndi yama shatta ndi Themba Ndi Themba
Amayesa kuti ifeyo ndi mphwemphwa
Anangodabwa ndangofika ndikubhebha
Trap yathu sungalowe chifukwa siiwe member
Iyi ndi yama Dada ndi Themba Ndi Themba Huh!

[Verse 1: Brainlock T-Kas]
Themba ndi shatta Themba ndi Don Dada
Themba ulemu amalandira ku Lusaka
Amamufila mu Ghetto anthu amamusata
Mumapusisana mukamati samatha
Themba pa den amamutchula Mbwindi
Themba nkazi wake ndiwo phula ndichi big
Themba ndi wachifumu koma samadya Kings
Themba Ghetto yinamudya koma Looks ya Dings
Tikufuna Themba! Tikufuna Drip!
Ukawona Thеmba Ndekuti wawona cheese
Themba ndi good boy Thеmba ndiwamu street
Themba boys yake sizamva ayi

[Verse 2: Nkhiwa]
Ooo oo
Themba Themba Themba ndi big stepper
Themba Themba Themba ndi big dripper
Mukapanga za themba mutsegula mmimba (ooh oh?)
Mukafuse mbali zakwanu Themba anthu amamuziwa
Themba ndi Wachilokolo koma amaziwa style
Sungamuyike mu botolo Themba ndiwamakani (makani)
Themba be the Reason Nkazi wako sakuyankha (kuyankha)
Machesi ali ndi ife nde Themba amangoyaka
Ooo oo boys yake sizamva (sizamva) ayi (ayi)
Themba anachotsa mantha walayi
Themba ndichi OG Themba sichi mphwemphwa
Themba sanena odi kwanu tizagenda

[Chorus : Brainlock T-Kas]
Mmh Yeah
Amayesa kuti ifeyo ndi mphwemphwa
Anangodabwa ndangofika ndikubhebha
Trap yathu sungalowe chifukwa siwe member
Iyi ndi yama shatta ndi Themba Ndi Themba
Amayesa kuti ifeyo ndi mphwemphwa
Anangodabwa ndangofika ndikubhebha
Trap yathu sungalowe chifukwa siiwe member
Iyi ndi yama Dada ndi Themba Ndi Themba Huh!

Themba ndi Themba Q&A

Who wrote Themba ndi Themba's ?

Themba ndi Themba was written by Brainlock T-Kas & Nkhiwa & Beats on Cortics & MEGa Beatz (MWI).

Who produced Themba ndi Themba's ?

Themba ndi Themba was produced by Nkhiwa & Beats on Cortics & MEGa Beatz (MWI).

When did Brainlock T-Kas & Nkhiwa release Themba ndi Themba?

Brainlock T-Kas & Nkhiwa released Themba ndi Themba on Wed Oct 04 2023.

Your Gateway to High-Quality MP3, FLAC and Lyrics
DownloadMP3FLAC.com