[Intro]
Dem bad
(Malawian)
Don't wake me up
Uh, uh, uh, uh
[Chorus]
Ngati zakumaloto
Ndamugwira nkono
Iyenso ali mommo ndangodabwa milomo
Muah, muah, muah, muah
Ngati zakumaloto
Ndamugwira nkono
Iyenso ali mommo ndangodabwa milomo
[Verse]
Sasuta mogo
Guy wina ati nono
Not too fast take it slow, slow
Bwera pafupi titenge photo
Kumu kisser pa forehead ati you the one
I wanna make you my only one
Number two ndindani chifukwa ndiwe number one
Nkazi wa bho ali ndi badman inenso ndadabwa
Nde umaipasa moto
Wandifaka mu bottle
Unedyo wa chi yao
Iwe nkazi waku mpoto
Pele pa tu ndi love sono, sono
I don't even know the meaning koma ndili m'momo
[Chorus]
Ngati zakumaloto
Ndamugwira nkono
Iyenso ali m'momo ndangodabwa milomo
Muah, muah, muah, muah
Ngati zakumaloto
Ndamugwira nkono
Iyenso ali m'momo ndangodabwa milomo
[Outro]
Sasuta mogo
Guy wina ati nono
Not too fast take it slow, slow
Bwera pafupi titenge photo
Kumu kisser pa forehead ati you the one
I wanna make you my only one
Number two ndindani chifukwa ndiwe number one
Nkazi wa bho ali ndi badman inenso ndadabwa
Nde umaipasa moto
Zakumaloto was written by Crispy Malawi & Horus Dem Bad.
Zakumaloto was produced by Horus Dem Bad.
Crispy Malawi released Zakumaloto on Sat Nov 30 2024.