[Chorus: Crispy Malawi]
Sungandisaize dancehall ina sintha singatalker sunathayime
I got some M's in the bank koma sindingakunyaditse
Ma cheese nde Ndi nyanja koma sindinga-
Sindingakubanditse
Sindingakubanditse
Sindingakubanditse
Sindinga-
[Verse 1: Crispy Malawi]
Ndiwe mfana woseketesa heavy sungandikwiyitse
Ndili ndi chimwana chi Beyoncé sungachithayime
Iwe Spe samafunika dzuwa kuti ashine (Shine)
Wavala watch ya bho koma ino ndi nthawi ya ine (Watch)
Palibepo baddie pa schedule pa ine
Koma utha kundi hitter ngati ndili online
Osandifunsa zoti ndingoyankha "I'm fine"
Mpatse mita Mandingo azayike pipe
[Verse 2: 60 Grams]
Ndungofila bho, Smokey wabwera pa Benz
Me and boys workin' palibepo za ulesi
You gotta lean after nangodyela cheese
They keep sayin' I'm crazy, told them that Phin is my G (G, G)
Can't mess with me mafana ndine wa street
I'm high on weed, can't give no attention to a bitch
Si iwe dolo ngati umalimbana ndine
Mafana a ulesi kukonda kupatsa busy
[Chorus: Crispy Malawi]
Sungandisaize dancehall ina sintha singatalker sunathayime
I got some M's in the bank koma sindingakunyaditse
Ma cheese nde Ndi nyanja koma sindinga-
Sindingakubanditse
Sindingakubanditse
Sindingakubanditse
Sindinga-
[Outro: Crispy Malawi]
Ten, twenty, thirty, forty, fifty, sixty
Ten, twenty, thirty, forty, fifty, sixty
Ten, twenty, thirty, forty, fifty, sixty
Yoghurt was written by Crispy Malawi & 60 Grams & Horus Dem Bad.
Yoghurt was produced by Horus Dem Bad.
Crispy Malawi released Yoghurt on Tue Nov 26 2024.