[Intro: Kineo Madness]
Yeah
Jah Knows Dem
Alright
[Chorus : Aidfest & Aidfest & Kineo Madness]
Umati yendabe, yendabe
Usatope usafooke (Usafooke)
Yendabe, yendabe
Usatope, usafooke
[Post-Chorus: Aidfest & Kineo Madness]
Ukafika, ukafikako
Ukafika, ukafikako
Ukafika, ukafikako
Ukafika, ukafikako
[Verse 1: Kineo Madness]
Ndawona sindingakwanitse, mene akupangira azinzanga
Awa anali [?] andidutsa pompaja
Mavuto andikakamira, mwayi wanditalikira
Komabe yendabe, yendabe
Ukagwa uzidzutse uzistsatse
Mavuto samatha mbale koma chilimikabe
Kakamiza adah, fumbi Ndi mwini adah
Palibe chovuta pa town[?] kuyenda mpaka kukafika
[Chorus : Aidfest & Aidfest & Kineo Madness]
Umati yendabe, yendabe
Usatope usafooke (Usafooke)
Yendabe, yendabe
Usatope, usafooke
[Post-Chorus: Aidfest & Kineo Madness]
Ukafika, ukafikako
Ukafika, ukafikako
Ukafika, ukafikako
Ukafika, ukafikako
[Verse 2: Aidfest Madness]
Sindinali chonchi Ine (Ine), koma chifukwa chamavuto ndimalimbika
And I don't wanna go back to the old days
Kumaziwa Pano ndinaphunzira
Za[?] sizilephera koma ife timayendabe
Olo katundu akulemera mavuto onse timasenzabe
Nde iwe yenda, yenda
Kholo ili ndiyawekha, wekha (Eya)
[Chorus : Aidfest & Aidfest & Kineo Madness]
Umati yendabe, yendabe
Usatope usafooke (Usafooke)
Yendabe, yendabe
Usatope, usafooke
[Post-Chorus: Aidfest & Kineo Madness]
Ukafika, ukafikako
Ukafika, ukafikako
Ukafika, ukafikako
Ukafika, ukafikako
Yendabe was written by Kineo Madness & Aidfest Madness & YOBA (MW).
Yendabe was produced by YOBA (MW).