Werenga by Faith Mussa (Ft. Madalitso Band)
Werenga by Faith Mussa (Ft. Madalitso Band)

Werenga

Faith Mussa & Madalitso Band

The music player is only available for users with at least 1,000 points.

Download "Werenga"

Werenga by Faith Mussa (Ft. Madalitso Band)

Release Date
Fri Jul 26 2019
Performed by
Faith MussaMadalitso Band
Produced by
Nico Bentley & Madalitso Band & Faith Mussa
Writed by
Faith Mussa & Nico Bentley & Yobu Maligwa & Yosefe Kalekeni

Werenga Lyrics

[Verse 1 : Faith Mussa & Madalitso Band]
Nane ndapambana chani Ine? (Ndapambana chani?)
Abale ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Madalitso mukundipatsawa (Ndapambana chani?)
Mbuye madalitso onsewa (Ndapambana chani?)
Ambuye ndapambana chani ine? (Ndapambana chani?)

[Pre-Chorus: Faith Mussa & Madalitso Band]
Oh Ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Madalitso mukundiwunjikira wo (Ndapambana chani?)
Ndikuchita kusowa kokatengera ine (Ndapambana chani?)
Oh Ndapambana chani ine? (Ndapambana chani?)
Ndapambana chani? Ine ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Oh Ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Ine Ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Oh Ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Oh Ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Oh Ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Ine ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Inu Madalitso onsewa (Ndapambana chani?)
Abale ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Oh Ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Ine ndapambana chani? (Ndapambana chani?)

[Chorus: Faith Mussa, Madalitso Band, Faith Mussa & Madalitso Band]
Werenga, werenga, werenga
Werenga, werenga, werenga madalitso ako
Oh madalitso ako (Madalitso ako)
Oh madalitso ako (Madalitso ako)
Werenga, werenga, werenga
Werenga, werenga, werenga madalitso ako
Oh madalitso ako (Madalitso ako)
Oh Madalitso ako (Madalitso ako)

[Pre-Chorus: Faith Mussa & Madalitso Band]
Oh Ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Ine Ndapambana chani ? (Ndapambana chani?)
Oh Ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Abale ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Oh Ndapambana chani?(Ndapambana chani?)
Oh Ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Eh Ndapambana chani?(Ndapambana chani?)
Abale ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Oh Ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Oh Ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Abale ndapambana chani ine? (Ndapambana chani?)
Abale ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Oh Ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Ine Ndapambana chani ? (Ndapambana chani?)
Ine Ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Ine Ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Ine Ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Oh ndapambana chani? (Ndapambana chani?)
Ine Ndapambana chani ? (Ndapambana chani?)

[Chorus: Faith Mussa, Madalitso Band,Faith Mussa & Madalitso Band]
Werenga, werenga, werenga
Werenga, werenga, werenga madalitso ako
Oh madalitso ako (Madalitso ako)
Oh madalitso ako (Madalitso ako)
Werenga, werenga, werenga
Werenga, werenga, werenga madalitso ako
Oh madalitso ako (Madalitso ako)
Oh Madalitso ako (Madalitso ako)
Iwe Madalitso ako
Madalitso ako, Madalitso ako
Iwe Madalitso ako
Madalitso ako

Werenga Q&A

Who wrote Werenga's ?

Werenga was written by Faith Mussa & Nico Bentley & Yobu Maligwa & Yosefe Kalekeni.

Who produced Werenga's ?

Werenga was produced by Nico Bentley & Madalitso Band & Faith Mussa.

When did Faith Mussa release Werenga?

Faith Mussa released Werenga on Fri Jul 26 2019.

Your Gateway to High-Quality MP3, FLAC and Lyrics
DownloadMP3FLAC.com