Uzithamanga by Crispy Malawi
Uzithamanga by Crispy Malawi

Uzithamanga

Crispy Malawi

The music player is only available for users with at least 1,000 points.

Download "Uzithamanga"

Uzithamanga by Crispy Malawi

Release Date
Wed Jan 10 2024
Performed by
Crispy Malawi
Produced by
BeatsByNice & Ayo Landie
Writed by
Crispy Malawi & BeatsByNice & Ayo Landie
About

Uzithamanga is a follow up of singles dropped by International Spe which includes Chabwino and International

Uzithamanga is the first single Dropped in 2024 by Spe, and was only premiered on YouTube via a lyric Visualiser

Uzithamanga Lyrics

[Intro]
Ayo Landie
Uzithamanga (huh huh)
Uzithamanga (hmm hmm)
Uzithamanga (iwe uyo)
Uzithamanga (Ay)

[Pre-Chorus]
Si iwe hule sizomango gona ku kacha (Ku culture!)
Uzidzuka Uzi thamanga thamanga
Sizomangolira ngati Mwana ukagwa (Ngaa)
Ukadzuka kusasa fumbi kumathanga
Utha kusuta kuti ugainy confi (Ha)
Koma Bola osathamanga
Sungathamange madzi atafika mkhosi (Ha)
Nde olo apapa ukhozano kungoyamba
Kuthamanga (Rah)

[Chorus]
Kumathanga (Go!)
Uzithamanga (uh huh)
Uzithamanga
Uzithamanga (huh)

[Verse]
Kuma talker promoter sindimadya exposure
Ati eh Spe unatha mantha (kumene)
Za ulere sindikupanga olo kamodzi
Mmmh man bolani kupanga zanga (Amen)
Olo Mpamba ine nditha kupatsa (Eh heh)
Koma ukasanja umapanga zotasa (Zoba)
Ine ndimapanga zomwe ndimafuna
Iwe umalandira zomwe amakupasa (CEO)
Basi busy mu hood kuzimva ushasha (Zoba)
Mafana opepela osadziwa Ku hasa (Zoba)
Business idea kuphwekesa Mogo kumapemphesa
Ana amu hood Kuwawopyeza

[Chorus]
Uzithamanga
Uzithamanga (iwe)
Uzithamanga
Uzithamanga

[Pre-Chorus]
Si iwe hule sizomango gona ku kacha (Ku Culture)
Uzidzuka Uzi thamanga thamanga (aaah Ase!)
Sizomangolira ngati Mwana ukagwa (Ngaa)
Ukadzuka kusasa fumbi kumathanga (sa sa sa sa sa)
Utha kusuta kuti ugainy confi (huh)
Koma Bola osathamanga (Osa ng'aza)
Sungathamange madzi atafika mkhosi (huh)
Nde olo apapa ukhozano kungoyamba
Kuthamanga

[Chorus]
Kumathanga (Rah)
Uzithamanga (Hu)
Uzithamanga (Hu)
Uzithamanga (Hu)

Uzithamanga Q&A

Who wrote Uzithamanga's ?

Uzithamanga was written by Crispy Malawi & BeatsByNice & Ayo Landie.

Who produced Uzithamanga's ?

Uzithamanga was produced by BeatsByNice & Ayo Landie.

When did Crispy Malawi release Uzithamanga?

Crispy Malawi released Uzithamanga on Wed Jan 10 2024.

Your Gateway to High-Quality MP3, FLAC and Lyrics
DownloadMP3FLAC.com