UMAKWANA SLiME by Lil Al, Em-EL (MWI) & 60 GRAM$
UMAKWANA SLiME by Lil Al, Em-EL (MWI) & 60 GRAM$

UMAKWANA SLiME

Lil Al * Track #5 On $LIME BUSINESS

The music player is only available for users with at least 1,000 points.

Download "UMAKWANA SLiME"

UMAKWANA SLiME by Lil Al, Em-EL (MWI) & 60 GRAM$

Performed by
Lil Al
Produced by
BISHOP 1800 & Famous The Soundgod
Writed by
Lil Al & EM-EL (MWI) & 60 Grams & BISHOP 1800 & Famous The Soundgod

UMAKWANA SLiME Lyrics

[Intro: Martin Meke]
Nde Pali kagulu aka kodabwitsa
Kamatchedwa ma slime, ati ma slime
Ahh ase "ati slime mentality, slime mentality"
Titanyamula tima cup tawo, ati basi kumatenga codeine kuphatikiza ndi sprite
Azimwa azikhala high hmm?
Ana opusa kwambiri
Nde timakhalatu kumavala Zima trouser dzazikulu
Kenako kumazikhwefulaso hmm?
Aah!
Ayo 1800

[Chorus: Lil Al]
Kumvela nyimbo zanga
Umakwana slime, umakwana
Top fan ati imangomvera nyimbo zanga
Umakwana slime, umakwana
Ati zimakape ziku biter ma concept anga
Umakwana slime, umakwana

[Verse 1: Em EL]
Yeah
Diso langa lafira chifukwa ndimabanda
Kamwana kakundi rider ngati Yokohama
Ana ohitter ife amapalasa mabwana (Mabwana)
Mumanama ma guy mumanama

[Verse 2: Lil Al]
Ndine dolo ngati madolo ali an zanga (Yeah)
Ndizitrapabe ndi gang yanga situdana (Yeah)
Vuto sine ngati gang yanu mulibe shasha
Mulowe flee market mukazigulire mpasha (Yeah)

[Verse 3: Em EL]
Kuposta nditatchena amangoti wow, wow, wow
Akuti "come give me dick right now, now
Yeah, Ganja yanga ndiya loud, loud
Phone ili pa DND ndangogweza sound

[Verse 4: 60 Grams]
Street nigga sindisekelera zachibwana
Ndimakonda zaza, drip zi ana ndi ndalama
Kakungondi yan'gana ndakafunsa what's up?
Eko handle sindikupatsa number yapa WhatsApp (WhatsApp)

[Verse 5: Lil Al]
Ayy wasteman sangakhale nzanga wa ine
Baddie a delete kaye IG kuti akhale mkazi wa ine (Wa ine)
Droppin' every week ndilibe nazo za timing
Za hard nthawi zonse ma opps zakudya rock climbin'

[Verse 6: Em EL]
Kakufuna Chanel, kakuwona ngati mdala wake ndi ineyo
Ati mpaka ndizikatengera ku hotel (Hotel?)
Kakufuna ku Breezer ine ndakagulira Doppel (Doppel)
Ati "Em-EL will you please be for real?"

[Verse 7: 60 Grams]
I started trappin' you boys ain't for real
Standin' on business forget a deal is a deal
I ain't stoppin' till I got a palm jive and that's good[?]
They be like "where you from" I be like my mothers womb (Yeah)
Ma hater ndi shit ndimawatampa ku loo
Ndima slimer overnight, tapanga set up chi stu

[Verse 8: Lil Al]
Yeah
Ndakachotsesa nyimbo za Aidfest Ndi Kineo (Kineo)
Mumanama ma guy, mumanama (Mumanama)
Faka , Lil Al, 60 Grams ndi achina Em EL
Umakwana slime, umakwana
Umakwana slime, umakwana

[Chorus: Lil Al]
Umakwana slime, umakwana
Umakwana slime, umakwana
Umakwana slime, umakwana
Umakwana slime, umakwana

[Outro: Lil Al ]
Sound god
Umakwana
Umakwana

UMAKWANA SLiME Q&A

Who wrote UMAKWANA SLiME's ?

UMAKWANA SLiME was written by Lil Al & EM-EL (MWI) & 60 Grams & BISHOP 1800 & Famous The Soundgod.

Who produced UMAKWANA SLiME's ?

UMAKWANA SLiME was produced by BISHOP 1800 & Famous The Soundgod.

Your Gateway to High-Quality MP3, FLAC and Lyrics
DownloadMP3FLAC.com