Ya ya yeah ah*4
(Eck)
Nane sindilola
Ndingofuna utandilola
(Hard Known Tiger)
Verse 1
Kunali chaku party
Kanali busy kumacheza ndi anzake
N'nakanika kuti mwina ndikathoke
Koma lero moni wokha ndikapatse
Muli bwanji ase
Kandiyang'ana mondikweza kunditsitsa
Ee ndati bwanji ase
Sumafuna ndi anthu ena kumacheza
Iwe usakhale ndiphuma
Ndikuuze zomwe mtima wandituma
Tipange love tandiyandikire
Kayang'ana molusa eti kamvekere
Ine bambo anga ndi abusa
Kundiona ndimwamuna amalusa
Msewu wake womwe uno amadutsa
Tandisiye ndimadana ndizopusa
Hook (Pex)
Name sindilola
Ndingofuna chabe baby utandilola
Daily sindikugona
Ndingofuna chabe baby utandilola
Daily ndikungolota
Tikusewera limodzi kunyanja
Bae ine sindilola
Ndingofuna chabe baby iwe utandilola
Bridge(Eck)
Oh no no noh no
Name sindilola
Oh no no no no no non
Ndingofuna utandilola yeah
Verse 2(Eck)
Mumtima mwanga nkhondo nkhondo ndiwe moto
Zondipatsa bondo bondo ine toto
Ndipatse chance love yanga ndikupatse
Uyilawe mtima pansi
Golide wanga
Mami wa ana anga
I really really love you more
I 'll never ever let you go
Kayambano kufewa
Ine ndasankha weyo mwaonsewa
Ndakapopa ndiwe ngelo
Kukafunsa dzina ati ndi Kalo
Ndimvetse kukoma new day
Ndalema kukhala kwa no bae
Daily daily ndikufuna ndizikuona
Ayi ayi zokuona ndikagona