[Intro: Suffix]
Wazizur
[Chorus: Driemo]
Si lero, si lero, si lero, si lero, si lero, si lero, si lero
Si lero, si lero, si lero, si lero, si lero, si lero, si lero
[Verse 1: Suffix & Driemo]
Si lero
Uluruwu ndiye sukuchoka
Cancer yi ngati ndingofa mwina ndizachila koma
Si lero
Ndaona zinthu ngati Doctor
Mmanjamu anthu kumangofa Ndufuna ntapuma koma
Si lero
I know lero sizingatheke
Pa wheelchair pa one day ndizachokapo
Inde ngakhale
Si lero
Masten anga kuli chete
Munapita ngati bodza nzakuonaninso ngakhale
[Chorus: Driemo]
Si lero, si lero, si lero, si lero, si lero, si lero, si lero
Si lero, si lero, si lero, si lero, si lero, si lero, si lero
[Verse 2: Suffix]
Mufunse Driemo
Made it outta Ntchisi ena nkumati si iyeyo
Nawenso uzaiphula aise ngakhale si lero
Nzothekanso kufa usanaiphulire ndiye moyo
Ma funso onse azayankhidwa ngakhale si lero
Wina akuyendera manja fukwa alibe miyendo
Amasamala ziweto
Suli wekha tiyeko
Ikanso ma earphone ndimvetsele mavutowa azatha ngakhale
[Chorus: Driemo & Choir]
Si lero, si lero, si lero, si lero, si lero, si lero, si lero
Si lero, si lero, si lero, si lero, si lero, si lero, si lero
[Outro: Kambwiri Sisters & Driemo]
Si lero (and I still believe)
Si lero (though not today)
Si lero(not today)
Si lero (not today)
Si Lero was written by Suffix (MWI) & Driemo.
Si Lero was produced by Savage on the Beat.
Suffix (MWI) released Si Lero on Thu May 23 2024.