Tiya, Tiya iwe Tiya ndimakukonda
Tiya, Tiya iwe Tiya ndimakukonda
Tiya, Tiya iwe Tiya ndimakukonda
Tiya, Tiya iwe Tiya ndimakukonda
Hehe! ndiwe wekha wokondedwa wanga, palibeso wina
Tiya, Tiya iwe Tiya ndimakukonda
Tiya, Tiya iwe Tiya ndimakukonda
Tiya, Tiya iwe Tiya ndimakukonda
Tiya, Tiya iwe Tiya ndimakukonda
[Interlude: Patrick Thim Sam]
Chonde ndimakudalira iweyo sweetheart wanga
Ndiweyo wekha basi
Osazandikhumudwitsa iyayi
Wachikondi wapamba Ndiweyo wekha basi
Ndikamakhala ndimadalira iweyo wekha basi
Tiya, Tiya iwe Tiya ndimakukonda
Tiya, Tiya iwe Tiya ndimakukonda
Tiya, Tiya iwe Tiya ndimakukonda
Princess wanga was written by Yobu Maligwa & Yosefe Kalekeni.
Princess wanga was produced by Madalitso Band.
Madalitso Band released Princess wanga on Fri Jun 13 2025.