Panado by Onesimus (MW)
Panado by Onesimus (MW)

Panado

Onesimus (MW) * Track #4 On Messenger

The music player is only available for users with at least 1,000 points.

Panado Lyrics

[Intro]
Panado, panado, mm, mm
Ma headache yeah, mm, mm
Panado, panado, mm, mm

[Verse 1]
Amakonda miseche
Amakonda munthu azivutika
Zochitika ngati siwopemphera
Daily, daily busy ntopoli
Kubaya ma damage
Kuwupatsa moyo wanga challenge
Machitidwe awo ngati Judas
Makhalidwe awo ngati njenjete

[Pre-Chorus]
Amafuna ndikokoloke
Amakhumbira nditapokoloka
Amafuna ndisokoloke
Amafuna mwina nditakomoka
Amafuna ndikokoloke
Amakhumbira nditapokoloka
Amafuna ndisokoloke
Amafuna mwina nditakomoka

[Chorus]
Ndi nsanje apatseni panado, panado
Panado, panado
Amweko panado, panado
Panado, panado (Yeah, yeah)

[Post-Chorus]
Munthu wakula ndi nsanje
Kaduka ndi nsanje
Kaduka mwina ndi nsanje
Kaduka, mtima wa chigawenga
Munthu wakula ndi nsanje
Kaduka ndi nsanje
Kaduka ndi nsanje
Kaduka, mtima wa chigawenga

[Verse 2]
Samafuna ndiyendere njale
Samakondwa ndikamadya money
Zikandiyendera amakoka chibale
Zikamandivuta andinyoza kumbali
Koma Mulungu wandichita balance, I relax
Amamenya nkhondo nditakhala pansi
Adani onse alemba m'madzi
Samakondwa nane

[Pre-Chorus]
Amafuna ndikokoloke
Amakhumbira nditapokoloka
Amafuna ndisokoloke
Amafuna mwina nditakomoka
Amafuna ndikokoloke
Amakhumbira nditapokoloka
Amafuna ndisokoloke
Amafuna mwina nditakomoka

[Chorus]
Ndi nsanje apatseni panado, panado
Panado, panado
Amweko panado, panado
Panado, panado (Yeah, yeah)

[Post-Chorus]
Munthu wakula ndi nsanje
Kaduka ndi nsanje
Kaduka mwina ndi nsanje
Kaduka, mtima wa chigawenga
Munthu wakula ndi nsanje
Kaduka ndi nsanje
Kaduka ndi nsanje
Kaduka, mtima wa chigawenga

[Outro]
Panado, panado
Ma headache, yah
Ma headache, yah
Panado, panado
Ma headache, yah
Ma headache, yah
Ma headache, ma headache, yah
Panado
Panado
Panado
Panado, panado
Panado
Panado
Panado, panado

Panado Q&A

Who produced Panado's ?

Panado was produced by Major 1 Records.

Your Gateway to High-Quality MP3, FLAC and Lyrics
DownloadMP3FLAC.com