[Intro]
Can I Talk To Ya
[Verse 1]
Sometimes i wish we learnt love in class back in high school
Maybe you and me right now we'd both know what to do
All forces are against us i wish love had instructions
But somehow i still choose you
Ngati madzi likandigwila ludzu
Ndikati gudyu gudyu
Umandichotsa khawa
Ndikati gudyu gudyu
I still want more of your love
[Verse 2]
M'mene undikondera baby ukufunika mendulo
Mene uwalila mum'dima undikumbutsa kendulo
Ka side chick nso ndika chani
Kwa chipha dzuwa ngati iwe
Iwe ndiwe MG1 2019 boma muyimenso
Ndikakhala ndimakondwera kuti iwe ndiwa ine
Ndikagwada ndimapephera Mulungu atidalitse
[Bridge]
Anthu akumachuluka nzeru
So many professors around you
Ena kutiona kuchita nselu
Ife tizingopanga zathu
You don' need no campaign
(no campaign)
[Chorus]
Ine ndakonda iwe (eh eh)
Ndafuna udziwe (eh)
No matter what they say (eh eh)
Ine ndakonda iwe (eh)
Wawina opanda campaign
No Campaign was written by Dali CITTY & Crack (MW).
No Campaign was produced by Crack (MW).
Dali CITTY released No Campaign on Mon Jan 01 2018.