[Chorus]
Utha kupeza wina koma sungapeze wina Ngati ine (Like me, like me, like me)
Utha kumamvana naye koma sungamvane nzomwe umvana ndi ine
Sine wanna be, life yanga ndima liva ngati ine
Pano mafana Amaimilira akafuna kukhala ngati Ine
[Verse]
Mesa ndukuuza nangobadwa chonchi sinachalire (I ain't forcing a bov trait)
Amangondimva nde zongonva kupwetekesa mutu matsire
Ndine Spe Chingaipe sine Maskal usadalire
You know I'm married to the money nde chibwezi chathu sichingalimbe
Dzulo BTz lero ndiku Mzuzu
Ofunika dhen Ku Kasungu ngati Kamuzu
Tili mu kitchen busy cooking ngati pun kasusu
(Malawian) Chichewa chikumveka Ngati Chizungu
Ati "Spe kodi walemba kapena Zungochoka Mmutu"
If it wasn't for this album nakangolemba buku
Pena ndimazimva ngati ndaziika ku nkhutu
Abale si T-shirt ndi a'ba.lé ndi mtundu
The community praying for more life ndi financial stability
The price went up mix nedzability
Funika more than one mita sindimaimba za charity, huh
[Chorus]
Utha kupeza wina koma sungapeze wina Ngati ine (Like me, like me, like me)
Utha kumamvana naye koma sungamvane nzomwe umvana ndi ine
Sine wanna be, life yanga ndima liva ngati ine
Pano mafana amaimilira akafuna kukhala ngati Ine
Ngati Ine was written by Crispy Malawi.
Ngati Ine was produced by Horus Dem Bad.
Crispy Malawi released Ngati Ine on Mon Nov 03 2025.