[Intro]
F9ine Entertainment
Mukauzane
Mukauzane
Mukauzane
Mukauzane
(Hm hm hm Malawian) Mukauzane
Mukauzane
Mukauzane
Mukauzane
[Chorus]
Ndungofuna kupota tsitsi
Ndungofuna kupota spliff
Zomwe ndikumaziwona ndikalota ndiza bho koma ndiza chisinsi
Ndungochilller pa corner easy, ku viber pachi loner
Middle finger to the other side, ndinavaya gang ina iku warmer[?] (Uh-huh)
[Post-Chorus]
Ma goat ndikulowetsa mu khola (Lowetsa)
Ma goat ndikulowetsa mu khola (Lowetsa)
Ma goat ndikulowetsa mu khola (Lowetsa)
Ma goat ndikulowetsa mu khola (Lowetsa)
Ma goat ndikulowetsa mu khola (Lowetsa)
Ma goat ndikulowetsa mu khola (Lowetsa)
Ma goat ndikulowetsa mu khola (Lowetsa)
Ma goat ndikulowetsa mu khola (Lowetsa)
[Verse 1]
Nde akumandi caller chifukwa ndina heater ngati solar
Nanga utafuna verse Spe koma kukanika chifukwa alibe dollar?
Iwe ine ndichi doba doba (Doba)
New Years Eve chaku Zomba (Zomba)
Beer Land mfana kuyilocker
Ndimagona mu tour bus ndili ndi energy sindukufuna kugona
Akucopela mene tikumovira dzulo amati zandibanda
Olo Landlord amadziwa kuti ife malo timalanda
From the bottom to the top uh-huh ankadziwa nda?
Ma verse angodzadza titha kuchotsa ziwanda
Jigi-Jigi-Jigi-Jigi iwe Spe mfana ndi chi C-E(O)
GOAT wanu sangamarke olo mwezi uli wonse atamadroppa
EP (Mbola), Album (Mbola), Mixtape (Mbola), Single (Mbola) uh-huh
Mpira uli ndi ine sangamarke ndi kape mwamva?
[Bridge]
Mukauzane
Mukauzane
Mukauzane
Mukauzane
[Chorus]
Ndungofuna kupota tsitsi
Ndungofuna kupota spliff
Zomwe ndikumaziwona ndikalota ndiza bho koma ndiza chisinsi
Ndungochilller pa corner easy kuviber pachi loner
Middle finger to the other side ndinavaya gang ina iku warmer[?] (Uh-huh)
[Post-Chorus]
Ma goat ndikulowetsa mu khola (Lowetsa)
Ma goat ndikulowetsa mu khola (Lowetsa)
Ma goat ndikulowetsa mu khola (Lowetsa)
Ma goat ndikulowetsa mu khola (Lowetsa)
Ma goat ndikulowetsa mu khola (Lowetsa)
Ma goat ndikulowetsa mu khola (Lowetsa)
Ma goat ndikulowetsa mu khola (Lowetsa)
Ma goat ndikulowetsa mu khola (Lowetsa)
[Verse 2]
Sponsor wanu awononga zi dollar
Mfana wakubanda tilanda bhola
Ndikufuna show ku North ma goat ali makola sali M'makola
Spe osamutola watentha inuyo mwapola
Chitseko nditha kutchyola, gang yonse ndikulowa (Nditha kutchyola)
Onsandibhowa (Onsandibhowa)
Mukauzane (Outro) was written by Crispy Malawi & F9INE (MWI) & Taks-Core.
Mukauzane (Outro) was produced by F9INE (MWI) & Taks-Core.
Crispy Malawi released Mukauzane (Outro) on Sat Jun 01 2024.