[Intro]
Ndikudziwa ndinachoka kale
Munandiona kale
(Eya kale, kale)
[Verse 1: Trappybeats.]
Ndinachoka kupita kutali
Kukasaka mwayi
(Amayi, amayi)
Ndikakumbuka munkanena
Zizandiyendera
Nkusintha moyo wanu mama
Ndinali mwana sindinkamvesa
Zoipa munkandilesa
Nkundilimbikisa mama
[Refrain: Trappybeats.]
Oh, oh, oh
Oh, oh, oh
Oh, oh, oh
[Verse 2: Hope Cizzle.]
Ndinakulonjezani mansion
Musanalandile pension
Ku suncity
Inu ndi bigman vacation
Koma osaona kuchedwa
Ndikuphusha zikutheka
Sooner or later
You will be eating my paper
It’s okay kaya ndigudumuka mumatope
Busy working all day
Cause I know my work is gonna pay off
It’s okay kaya ndigudumuka mumatope
Busy working all day
Cause I know my work is gonna pay off
[Refrain: Trappybeats.]
Oh, oh, oh
Oh, oh, oh
Oh, oh, oh
Mama was written by Trappybeats. & Hope Cizzle..
Mama was produced by Trappybeats..
Trappybeats. released Mama on Mon Oct 27 2025.