Kwanu Nkwanu by Suffix (MWI)
Kwanu Nkwanu by Suffix (MWI)

Kwanu Nkwanu

Suffix (MWI) * Track #12 On Before I Sleep

The music player is only available for users with at least 1,000 points.

Kwanu Nkwanu Lyrics

[Intro:]
Listen

[Verse 1:]
Bambo anga ankandikhazika
Pansi, ndili mwana wovuta
Ndili chakusekondale heee ndisakuganizaso zoyimba
Mwana wanga ndithu kukula
Ife taonapo yambili mvula
Ndiwe first born ife tikudalila, ukafuntha uzapita mwachangu kumanda
Kusukulu komwe uliko, uzikumbuka komwe uchokela
Nanenso nnali ndiazizanga ambili sindziwa komwe analowela

[Chorus:]
Dziwa dziwa dziwa, mwana wanga
Dziwa dziwa dziwa, mwana wanga
Dziwa dziwa mwana wanga
Dziwa dziwa, mwana wanga
Kwanu nkwanu nkwanu
Mwana wanga, kwanu nkwanu nkwanu
Mwana wanga, kwanu nkwanu
Mwana wanga, kwanu nkwanu nkwanu
Mwana wanga
Heeehhh

[Post-Chorus:]
Hee huhu
Hee huhu
Hee huhu
Hee huhu

[Verse 2:]
Yea, life sikhala fair
Macritisism sabweletsa sheda
Aliyense ali nzokonda zake, akadana ndizokonda zako usamawatengela
Kumasiyanitsa azako ndiabale
Ena utavutika sangathandize m'bale
Osamatengeka akamakuchemelera
Enawo Ukazazizila azakupanga chandamaleee

[Chorus:]
Dziwa dziwa dziwa, mwana wanga
Dziwa dziwa dziwa, mwana wanga
Dziwa dziwa mwana wanga
Dziwa dziwa, mwana wanga
Kwanu nkwanu nkwanu
Mwana wanga, kwanu nkwanu nkwanu
Mwana wanga, kwanu nkwanu
Mwana wanga, kwanu nkwanu nkwanu
Mwana wanga
Heeehhh

[Post-Chorus:]
Hee huhu
Hee huhu
Hee huhu
Hee huhu

[Outro:]
Dziwa dziwa dziwa, mwana wanga
Dziwa dziwa dziwa, mwana wanga
Dziwa dziwa mwana wanga
Dziwa dziwa, mwana wanga
Kwanu nkwanu nkwanu
Mwana wanga, kwanu nkwanu nkwanu
Mwana wanga, kwanu nkwanu
Mwana wanga, kwanu nkwanu nkwanu
Mwana wanga
Heeehhh

Your Gateway to High-Quality MP3, FLAC and Lyrics
DownloadMP3FLAC.com