It's Nyce, F9INE Entertainment
I know, I know, I know, I know
Kuti kakhala (komaliza)
Ayayayaya (Malawian), Mmh
[Chorus]
Umangowona kundinyaditsa (Komaliza) (Aah Ah)
Ndine amene ndima kukwanitsa (Komaliza) (Aah Ah)
Ngati zathapo chabwino komaliza (Komaliza) (Aah Ah)
Ndipatse chance komaliza (Komaliza) (Aah Ah)
Chabwino ndingogunditsa (Komaliza) (Aah Ah)
Ati Spe "Bwanji umandivutitsa" (Komaliza) (Aah Ah)
"Ndikakulola basi uzindipusitsa" (Komaliza) (Aah Ah)
"Ukandihuga basi uzindikissa" (Komaliza) (Aah Ah)
"Koma pa net tima babe ena ukumawa hitter" (Komaliza) (Aah Ah)
Haa Eh Chabwino basi ndasiya (Komaliza) (Aah Ah)
Mangofuna ndika stresser uzili njanjitsa (Komaliza) (Aah Ah)
Ndilipa top pamwamba pakopa sinditsika (Komaliza) (Aah Ah)
Ndimadana ndi zondipusitsa (Komaliza) (Aah Ah)
[Verse]
Kodi Bwanji? uli ndi ine olo pa msika?
Si iwe mtengo koma nditha kukwera ndi ku kutsika
Ndamenya shot kuti Nkhani ndingozifupikitsa
Round one, two titha kumenya molumikiza
[Chorus]
Umangowona kundinyaditsa (Komaliza) (Aah Ah)
Ndine amene ndima kukwanitsa (Komaliza) (Aah Ah)
Ngati zathapo chabwino komaliza (Komaliza) (Aah Ah)
Ndipatse chance komaliza (Komaliza) (Aah Ah)
Chabwino ndingogunditsa (Komaliza) (Aah Ah)
Ati Spe "Bwanji umandivutitsa" (Komaliza) (Aah Ah)
"Ndikakulola basi uzindipusitsa" (Komaliza) (Aah Ah)
"Ukandihuga basi uzindikissa" (Komaliza) (Aah Ah)
"Koma pa net tima babe ena ukumawa hitter" (Komaliza) (Aah Ah)
Eh Chabwino basi ndasiya (Komaliza) (Aah Ah) (Siya) (Siya)
Mangofuna ndika stresser uzili njanjitsa (Komaliza) (Aah Ah)
Ndilipa top pamwamba pakopa sinditsika (Komaliza) (Aah Ah)
Ndimadana ndi zondipusitsa (Komaliza) (Aah Ah)
[Outro]
(Komaliza), Komaliza
Komaliza
Komaliza
Komaliza was written by Crispy Malawi & F9INE (MWI) & BeatsByNyce.
Komaliza was produced by F9INE (MWI) & BeatsByNyce.
Crispy Malawi released Komaliza on Thu Mar 28 2024.