[Intro: Sho Madjozi]
Moni, moni, moni
Kuyilowa ndi mutu
Halo, ndasiya mudothi
(Mayazi, mayazi, mayazi)
Iyho
[Pre-Chorus: Sho Madjozi]
Mayazi, mayazi, mayazi
Gwira malaya nane ndi ilowe basi
Mayazi, mayazi, mayazi
Nkhani ya manyado libe nkhala pakati
Mayazi, mayazi, mayazi
Kuyilowa ndi mutu mopanda manyazi
Mayazi, mayazi, mayazi
Okudya ndalama samatcheka balansi
[Chorus: Sho Madjozi]
Vina
Tchola
Tshika
Kadigong
Kadi-kadi, kadigong
Kadi-kadi, kadigong
Vina
Tchola
Tshika
Kadigong
Kadi-kadi, kadigong
Kadi-kadi, kadigong
Vina
Tchola
Tshika
Kadigong
Kadi-kadi, kadigong
Kadi-kadi, kadigong
Vina
Tchola
Tshika
Kadigong
Kadi-kadi, kadigong
Kadi-kadi, kadigong
[Verse 1: Sho Madjozi]
Sinali plani kuti ndikukonde (Koma)
Watshekemela ngati ndiwe combe (Ona)
Watseleekeza ma guy wonse
Odi ndi ka pote
Tizitchiiilla tiKhale Pa easy
Ndili ndi mandede ngati lani lizzi
Ndimakoonda njonda zachimidzi
A'khale wauleemu opanda utchissi
Tenga u'moodzi tinyowe kukhosi (Nane ndima nyowa uka kamba zaku khosi)
Ndikutengele ku Jhoni u kawone tshotshi (Jozi)
Ukazipeza ndi achina Sho Madjozi (Konkoo)
Ndilibe phuma ndine nkazi wodeekha
Koma ndi Kabwella undivulile wekha
Mfana woteentha ta ziiyiteleka
Kumayi chakulila ndika mayi peleka
[Refrain: ]
I-yeah, yah-hah-hah
I-yeah, yah-hah-hah
Ayah-yah-yah, yah-hah
Ayah-yah-yah, yah-hah
[Chorus: Sho Madjozi]
Vina
Tchola
Tshika
Kadigong
Kadi-kadi, kadigong
Kadi-kadi, kadigong
Vina
Tchola
Tshika
Kadigong
Kadi-kadi, kadigong
Kadi-kadi, kadigong
[Verse 2: Gemini Major]
Mkazi wakunja khalidwe lachimalawi
Ndipanga naye chani fukwa ndine mphawi
Nyumba yakwawo yaku mayadi
Makolo akachoka timapanga party
Chikondi cha season ngati mtengo wa mango
Koma ndatopa nane ndikhale wako
Uzi ndigwira gwira ngati kupanga chipako
Polama pango'no undigwiritse thako
Ndikukwatile kapena tipange chinkhoswe
Olo ndidzidya mwa chinsinsi ngati khoswe
Dona ya ulemu Ndipo alibe chipongwe
Ndimupatse mimba kuti akhale pakhonde
Wabwera ndi Bola odi ndikapote
Tikawone Nyanja Ng'ona ku Liwonde
Kukunyaditsa kuti akuwone
A Nsanje kaduka onse aku zonde
[Chorus: Sho Madjozi]
Vina
Tchola
Tshika
Kadigong
Kadi-kadi, kadigong
Kadi-kadi, kadigong
Vina
Tchola
Tshika
Kadigong
Kadi-kadi, kadigong
Kadi-kadi, kadigong
Vina
Tchola
Tshika
Kadigong
Kadi-kadi, kadigong
Kadi-kadi, kadigong
Vina
Tchola
Tshika
Kadigong
Kadi-kadi, kadigong
Kadi-kadi, kadigong
[Refrain: ]
I-yeah, yah-hah-hah
I-yeah, yah-hah-hah
Ayah-yah-yah, yah-hah
Ayah-yah-yah, yah-hah
Kadigong was written by Sho Madjozi & Gemini Major & Ntando Yamahlubi.
Kadigong was produced by Gemini Major & Exclusive Drumz.
Sho Madjozi released Kadigong on Fri Oct 04 2024.