Oti$ DEaN III
Oti$ DEaN III
Oti$ DEaN III & Zayshan
Oti$ DEaN III & Jyc9 jr
Oti$ DEaN III & ThxtBoyRoy
Oti$ DEaN III & Shazzie
Oti$ DEaN III
Oti$ DEaN III & Shazzie
Oti$ DEaN III & Jyc9 jr
Oti$ DEaN III &
[Verse 1: Oti$ DEaN III]
Ukasekelera, ukamwetulira
Ine thupi lonse nthumazi
Sindikufuna wachikondi wina
Koma iweyo basi
Ukangodiyandikira
Ine zonse kayale
Ukangondinong'oneza
Nzelu zonse balala
Chifukwa cha iwe
[Pre-Chorus: Oti$ DEaN III]
Sinditha kumvetsa
Sinditha kumvetsa
Kodi zinakhala bwanji
Lelo ndamupeza
Lelo ndamupeza
Wanga wanga wachikondi
Muntima ndimanyadira
Chifukwa cha iwe
Umandikwanira
Pa iwe ndinathera
[Chorus: Oti$ DEaN III]
Ulibe competition-ih
Wawina kale
Chikondi chopanda season-ih
Ndichomwe tilinacho ife
Ooh-oh x4
Iwe ndi ine mpaka kalekale
Ooh-oh x4
Iwe ndi ine sitingasiyane
[Verse 2: Jyc9 jr]
Chikondi chokoma ngati Candy
Palibenso wina angalande
Palibenso wina angamake
Iwe ndi ine nde mpaka kalekale
Ndaima pachulu aliyense adziwe
Mwaiwe ndapeza chikondi chamuyaya
Sitizalekana baby sindizakutaya
Ntima wanga wakana kukonda wina
[Pre-Chorus: Oti$ DEaN III]
Sinditha kumvetsa
Sinditha kumvetsa
Kodi zinakhala bwanji
Lelo ndamupeza
Lelo ndamupeza
Wanga wanga wachikondi
Muntima ndimanyadira
Chifukwa cha iwe
Umandikwanira
Pa iwe ndinathera
[Chorus: Oti$ DEaN III]
Ulibe competition-ih
Wawina kale
Chikondi chopanda season-ih
Ndichomwe tilinacho ife
Ooh-oh x4
Iwe ndi ine mpaka kalekale
Ooh-oh x4
Iwe ndi ine sitingasiyane
[Brigde: Oti$ DEaN III]
Iweyo ndi ineyo
Paliponse kuyenda Shosholo
Iweyo ndiwe MG1
Usamakaikire
Moyowu siungatheke
Kukhala opanda iwe
[Chorus: Oti$ DEaN III]
Ulibe competition-ih
(Eeeeeeeeeeeh)
Wawina kale
Chikondi chopanda season-ih
(Chopanda season-ih-ih-ih-iiih)
Ndichomwe tilinacho ife
(Tilinacho Ife)
Ooh-oh x4
Iwe ndi ine mpaka kalekale
Ooh-oh x4
Iwe ndi ine sitingasiyane
Iwe Ndi Ine was written by Jyc9 jr & Oti$ DEaN III.
Iwe Ndi Ine was produced by Gxfted.
Oti$ DEaN III released Iwe Ndi Ine on Thu Mar 21 2019.