Kell Kay
Kell Kay & Suffix (MWI)
Kell Kay & Mfumu Hyphen & Tuno (MWI)
Kell Kay & The Black Missionaries
Kell Kay & Teddy Makadi & The Kambwiri Sisters
Kell Kay & The Great Angels Choir (MW)
Kell Kay & Saint Realest
Kell Kay
Kell Kay & Zani Challe
Kell Kay & The Kambwiri Sisters &
Kell Kay
Kell Kay
Kell Kay
Kell Kay & Lucius Banda & Lulu (MWI)
Kell Kay
Kell Kay
Kell Kay & Leslie (MWI)
In Love is the 7th Song on Album Ndabwera Ndi Nkhani
This romantic melodic song features R&B Singer Teddy and Kell Kay’s Sisters Chinsisi and Chisomo (The Kambwiri Sisters) who do the background vocals and outro
The song is produced by Henwoood
[Verse 1: Teddy MW]
Umangofuna tizicheza
Paja umati ndimakuseketsa
Tikamayenda kwa Milesa
Anthu amangotisekelera
[Chorus: Teddy MW]
Am I really in Love with You?
Pena umangodipepelesa
Am I really in Love with You?
Pena umangodipepelesa
[Verse 2: Kell Kay]
Sindingakugawane ndi wina
Kodi mawu aku lonjeza
Nanga utaponda polakwika
Ungadiuze ndisamale?
Zomaswerana mtima
Kundiuza ndiyiwale
Ku lonjeza zosatheka mulibe mwako mu dikishonale
Remember utagwada kuti ndidalire
Unkati udzandikwatira kuti ndi dikirebe
[Chorus: Kell Kay & Kambwiri Sisters]
Are you really in Love with me?
Olo Ukumangodipepelеsa
Are you really in Love with mе?
Olo nawe ukunditayitsa
Are you really in Love with me?
Olo ukumangodipepelesa
Are you really in Love with me?
Olo nthawi ukunditayitsa
[Verse 3: Teddy MW]
Chikondi chako
Sindichiwona baby momwe uchikambira
Chimandi talikira
Ndipo mawu anga wako
Amangosintha baby wakhumbira
Ine nkhawi bii!!!
[Chorus: Teddy MW, Kell Kay & Kambwiri Sisters]
Are you really in Love with me?
Olo Ukumangodipepelesa
Are you really in Love with me?
Olo nawe ukunditayitsa
Are you really in Love with me?
Olo ukumangodipepelesa
Are you really in Love with me?
Olo nthawi ukunditayitsa
[Outro: Kambwiri Sisters]
(Umangodi umayi)
(Umangondipepelesa)
(Umangodi umayi)
(Umangondipepelesa) are you really in love with me?
Olo ukumangodipepelesa
Are you really in love?
Olo ukumangodipepelesa
Are you Really in Love?
In Love was written by Kell Kay & Teddy Makadi & Henwood & Chinsinsi Kambwiri & Chisomo Kambwiri.
In Love was produced by Henwood.