Chimwana Changa by Praise Umali & Faith Mussa
Chimwana Changa by Praise Umali & Faith Mussa

Chimwana Changa

Praise Umali

The music player is only available for users with at least 1,000 points.

Download "Chimwana Changa"

Chimwana Changa by Praise Umali & Faith Mussa

Release Date
Fri Jul 25 2025
Performed by
Praise Umali
Produced by
Praise Umali & Faith Mussa & Daniel Khoviwa
Writed by
Praise Umali & Faith Mussa

Chimwana Changa Lyrics

[Intro]
Mayo! chalowelera! (Chalowelera dele!)
Mayo! chimwana changa dele, Mayo! chalowelera (Chalowelera dele!)
Mayo! chimwana changa dele, Mayo! chalowelera! (Chalowelera dele!)
Mayo! chimwana changa dele, Mayo! chalowelera (Chalowelera dele!)
Mayo! chimwana changa dele, Mayo! chalowelera! (Chalowelera dele!)
Mayo! chimwana changa dele, Mayo! chalowelera (Chalowelera dele!)

[Verse 1: Faith Mussa]
Mwana wanga ukupita (Iwe! Iwe, Iwe)
Chimwemwe Ndi chisoni (Iwe! Iwe, Iwe)
Zagwira mtima wangawu (Iwe! Iwe, Iwe)
Times are bad and we know that
Pamene ndingoyimba

[Chorus: Faith Mussa]
(Mayo! chimwana changa dele, Mayo! chalowelera!)
Iwe kumakapemphera uko (Mayo! chimwana changa dele, Mayo! chalowelera!)
Sinkufuna ndizalire mwana wanga ine (Mayo! chimwana changa dele, Mayo! chalowelera!)
Osati chalowelera dele (Mayo! chimwana changa dele, Mayo! chalowelera!)
Ndati kumakapemphera uko! (Mayo! chimwana changa dele, Mayo! chalowelera!)
Usakalowelere(Mayo! chimwana changa dele, Mayo! chalowelera!)
Osati chalowelera dele (Mayo! chimwana changa dele, Mayo! chalowelera!)
Sinkufuna ndizalire mwana wanga ine (Mayo! chimwana changa dele, Mayo! chalowelera!)

[Verse 2: Praise Umali]
Kumene ukupita uko (Iwe! Iwe, Iwe)
Iwe ukadzasochera ah (Iwe! Iwe, Iwe)
Mh, mwana wanga follow the light, iwe (Iwe! Iwe, Iwe)
Iwe follow the fire
Pamene ndikuyimba

[Chorus: Praise Umali]
(Mayo! chimwana changa dele, Mayo! chalowelera!)
Mwana wanga don't forget to pray (Mayo! chimwana changa dele, Mayo! chalowelera!)
I don't wanna lose you(Mayo! chimwana changa dele, Mayo! chalowelera!)
Iwe udzikapemphera uko, Iwe kumakapemphera uko (Mayo! chimwana changa dele, Mayo! chalowelera!)

[Outro: Faith Mussa]
Papapa (Mayo! chimwana changa dele, Mayo! chalowelera!)

Iwe kumakapemphera uko
Osati chalowelera dele

Chimwana Changa Q&A

Who wrote Chimwana Changa's ?

Chimwana Changa was written by Praise Umali & Faith Mussa.

Who produced Chimwana Changa's ?

Chimwana Changa was produced by Praise Umali & Faith Mussa & Daniel Khoviwa.

When did Praise Umali release Chimwana Changa?

Praise Umali released Chimwana Changa on Fri Jul 25 2025.

Your Gateway to High-Quality MP3, FLAC and Lyrics
DownloadMP3FLAC.com