Chabwino by Crispy Malawi
The music player is only available for users with at least 1,000 points.

Download "Chabwino"

Chabwino by Crispy Malawi

Release Date
Sat Nov 25 2023
Performed by
Crispy Malawi
Produced by
BeatsByNice & Ayo Landie
Writed by
Crispy Malawi & Ayo Landie & BeatsByNice

Chabwino Lyrics

[Intro:Bob Marley & Crispy Malawi]
That's Nice
Are you a rich man?
What you mean rich, what ya mean?
You have a lot of possessions? Lot of money in the bank?
Possessions make you rich?
I don't have that type of richness
My richness is life
Malawian
Ayo Landie
Ayy

[Chorus]
Chabwino moyo wambiri moyo wabwino (More life)
Anthu ena Alibe pabwino
Ndekumangothokoza ukakhala pabwino (Okay)(How?)
From Capetown to Cairo (Phew)
Funa Kuthamangitsa ma File
Bars ili sharp ngati mpaliro (sharp)
Siza escape from Sobibor

[Verse: Crispy Malawi]
Phone ndima user apple (iPhone) (iPhone)
The bros go wherever I go (I go) (I go)
Ndimashala Ku Chinsapo (Chinsapo) (Chinsapo)
Ndi Hood yovutirapo (Mmmh hmmm)
I got Fifteen niggas mu bedsitter (Okay)
Olo ma neighbour amadziwa Ndine o hitter (Let's go)
Tungosuta Zaza ngati osowa zochita (mmmh hm)
Koma business talk ikumayambira six figurеs
Nali Ku Gava anali Ku Bambino (Okay)
Rich mamie ndimangosonkhako ma riddle (ooh oh)
Akut Spe you got bars ngati Bwandilo (ayaya)
Mfana wa sick kumusamala ngati namwino
Si inе ophula koma life ili pa bwino (Life is good)

[Chorus]
Moyo wambiri moyo wabwino (More life)
Anthu ena Alibe pabwino
Ndekumangothokoza ukakhala pabwino (okay)(How?)
From Capetown to Cairo (Phew!)
Funa Kuthamangitsa ma File
Bars ili sharp ngati mpaliro (sharp)
Siza escape from Sobibor

[Outro]
Phone ndima user apple (iPhone) (iPhone)
The bros go wherever I go (I go) (I go)
Ndimashala Ku Chinsapo (Chinsapo) (Chinsapo)
Ndi Hood yovutirapo
Mmmh hmmm
Mmmm mmm
Okay
We ain't got no time
(Spe!) (Spe!)

Chabwino Q&A

Who wrote Chabwino's ?

Chabwino was written by Crispy Malawi & Ayo Landie & BeatsByNice.

Who produced Chabwino's ?

Chabwino was produced by BeatsByNice & Ayo Landie.

When did Crispy Malawi release Chabwino?

Crispy Malawi released Chabwino on Sat Nov 25 2023.

Your Gateway to High-Quality MP3, FLAC and Lyrics
DownloadMP3FLAC.com