[Intro]
Dem Baad
Dem baddies
Yeah
[Chorus]
Lisa Amandibalalisa
Mercy Akuti sangadyese
Jesse akati agwedeze
Utha ku Spenda Ndalama Zonse
Praise Akufunika Benz
Aggie Akufunika Kheshi
Ya i phone, nails ndima Ma Mesh
Ndi blessor oti Azilipira Rent
Ine Benz, ndikufunika Benz
Benz, ndikufunika Benz
Benz, ndikufunika Benz
Benz ndikufuna Benz
[Verse]
Ndi Good Girl amangofuna Vepi
Ma Bwana amangomutsitsa Dress
Nde friend akuvaila Nurse
Kuti azingophaka Plain
Muzifunsa Musanapange Date
Mandem anagwira nazo Ex
Ataziwa anali ndima Stress
Nde anangoyamba Ku Hater wezi wezi
Dollar zanu osamangomwera Best
Zina kumapangako invest
More Profits, kuchepesa Ma regrets
Kuchulusa ma returns
[Chorus]
Lisa Amandibalalisa
Mercy Akuti sangadyese
Jesse akati agwedeze
Utha ku Spenda Ndalama Zonse
Praise Akufunika Benz
Aggie Akufunika Kheshi
Ya i phone, nails ndima Ma Mesh
Ndi blessor oti Azilipira Rent
Ine Benz, ndikufunika Benz
Benz, ndikufunika Benz
Benz, ndikufunika Benz
Benz ndikufuna Benz
[Outro]
Ndikufunika Benz
Ndikufuna Benz
Benz was written by Crispy Malawi & Horus Dem Bad.
Benz was produced by Horus Dem Bad.
Crispy Malawi released Benz on Sat Nov 30 2024.