[Verse 1: Theresa Phondo]
Zaka zambiri zatha
Iwe ine tikucheza
Mphekesela zinkamveka kuti ife ndi chibwezi
Koma ife tinkakana
Timvekere sizingatheke
Iwe ndi ine sitilola
[Pre-Chorus: Theresa Phondo]
Lero ndatopa ndimafunso omadzifunsa ndekha
Ine ndalema ndimafunso ondifunsaso ena
Chifukwa chomwe ndimadziwa nchoti ndimakukonda
Chimodzi chomwe n'funa n'dziwe
Ndimve pakamwa pako
[Chorus: Theresa Phondo]
Ngati umandikondadi ine
Umandifunadi ine?
Ndimafuna ndidziwe
Ndidziwe, ndidziwe
Ndimafuna ndidziwe
Ndidziwe, ndidziwe
[Verse 2: Kelvin Sings]
Nthawi nde ikupita
Nkhawa nde zikubwerabe (bwerabe)
Chovuta kodi nchani kunena m'mene umamvera, yeah
I need some assurance
Munthune ndikukula, yeah
Nde tangonena tipange ma plan kuti zinthu zikhala bwanji
[Pre-Chorus: Theresa Phondo & Kelvin Sings]
Poti ndatopa ndimafunso omadzifunsa ndekha
Ine ndalema ndimafunso ondifunsaso ena
(Oh) Chifukwa chomwe ndimadziwa nchoti ndimakukonda
(Iwe ndi amene ndimakonda)
Chimodzi chomwe n'funa n'dziwe
Ndimve pakamwa pako
[Chorus: Theresa Phondo & Kelvin Sings]
Kodi umandikondadi iwe
Oh, umandifunadi iwe
Ndimafuna ndidziwe
Ndidziwe, ndidziwe
Ndimafuna ndidziwe
Ndidziwe, ndidziwe
Oh, umandikondadi iwe?
Umandikondadi iwe?
Ndimafuna ndidziwe
Ndidziwe, ndidziwe
Ndimafuna ndidziwe
Ndidziwe, ndidziwe
[Outro: Theresa Phondo & Kelvin Sings]
Ndidziwe, ndidziwe, ndidziwe
(Patseko assurance)
Ndimafuna ndidziwe
Ndidziwe, ndidziwe
(Munthune ndikukula)
Ndidziwe, ndidziwe, ndidziwe
(Patseko assurance)
(Munthune ndikukula)
Ndimafuna ndidziwe
Ndidziwe, ndidziwe
(Patseko assurance)
(Munthune ndikukula)
Theresa-phondo released Assurance on Tue May 03 2022.