[Verse 1]
A Phiri Anabwera kuchoka ku Harare
A Phiri Anabwera kuchoka ku Harare
Pobwera kumeneko anabwera ndi suitcase
Pobwera kumeneko anabwera ndi suitcase
Koma mkati mwa suitcase munalibe kanthu shuwa
Ndati mkati mwa suitcase munalibe kanthu shuwa
[Pre-Chorus]
A Phiri anaganiza "kodi ndidzayenda kuti?"
Makolo anga onse anamwalira ku Dara
A Phiri anaganiza "kodi ndidzayenda kuti?"
Makolo anga onse anamwalira ku Dara
Koma mkati mwa suitcase munalibe kanthu shuwa
Ndati mkati mwa suitcase munalibe kanthu shuwa
A Phiri anaganiza "kodi ndizayenda kuti?"
Makolo anga onse anamwalira ku Dara
A Phiri anaganiza "kodi ndizayenda kuti?"
Makolo anga onse anamwalira ku Dara
[Chorus]
A Phiri eh
A Phiri eh
A Phiri eh
A Phiri eh
A Phiri eh
A Phiri eh
A Phiri eh
A Phiri eh
A Phiri eh
[Pre-Chorus]
A Phiri anaganiza "kodi ndizayenda kuti?
A Phiri anaganiza "kodi ndizayenda kuti?
Ndati Phiri anaganiza "kodi ndizayenda kuti?
Koma mkati mwa suitcase munalibe kanthu shuwa
[Chorus]
A Phiri eh
A Phiri eh
A Phiri eh
A Phiri eh
A Phiri eh
A Phiri eh
Aphiri was written by Faith Mussa & Nico Bentley.
Aphiri was produced by Nico Bentley.
Faith Mussa released Aphiri on Fri Jul 26 2019.