Sake

Clovix

The music player is only available for users with at least 1,000 points.

Download "Sake"

Sake by Clovix

Performed by
Clovix

Sake Lyrics

Eh

Eh....

Mwana  usadande (aaaah)
Mwananga usadande
Eh mwananga usadande

Mi  work hard 6 to 6 (for your sake)
Kumangidwa  ndi a police(For your Sake)
Kupangaso risky business (For your sake)
Fighting  that one makes you stress(For your sake)
Hustlin all day n night (For your sake)
Staying awake late @ night (for your Sake)
Everything for you baby (baby)
Just  fi yah good life baby

For your sake oh lelelele....(my baby)
For your sake oh no eh....(x2)

Ofcourse singathe kupanga zonse (baby) Koma sindingaleke (baby)
Kugwira ntchito molimbika zofunika Everyday zipezeke
Singathe kukupatsa ine zonse(baby) koma sindingaleke(baby)
Kugwira ntchito molimbika someday khumbo lako lizatheke

Working hard 6 to 6 (For your sake)
Kumangidwa ndi a police (For your sake)
Kupangaso risky business (For your sake)
Fighting that one makes you stress (For your sake)
Hustlin all day n night (For your sake)
Staying awake late @ night (For your sake)
Olo nditadwala sindimafokabe
Mi still hustle hard

As long as I live
Ndiziyetsetsa mbali yanga kuti uzikhala okondwa
As long as I live
Ndikulonjeze mwana wanga moyo mwako sinzachoka
Pena ndimakukhumudwitsa
Udindo wanga simaukwanitsa
Nane ndine munthu ndili ndi zofooka
But fi yah good ndiyetsetsa osafoka

For your sake oh lelelele....
For your sake oh no eh....(x2)

Ofcourse singathe kupanga zonse Koma sindingaleke
Kugwira ntchito molimbika zofunika Everyday zipezeke
Singathe kukupatsa ine zonse koma sindingaleke
Kugwira ntchito molimbika someday khumbo lako lizatheke

Working hard 6 to 6 (For your sake)
Kumangidwa ndi a police (For your sake)
Kupangaso risky business (For your sake)
Fighting that one makes you stress (For your sake)
Hustlin all day n night (For your sake)
Staying awake late @ night (For your sake)
Olo nditadwala sindimafokabe
Mi still hustle hard

For your sake lelelele....
For your sake oh no eh...

....The End....
Artist : Clovix
Song : Sake
Produced by Taktic (Frame City Rich)

A 2019 Karbon Clan & The Tag Team presentation

Your Gateway to High-Quality MP3, FLAC and Lyrics
DownloadMP3FLAC.com